Tito 1
1 PAULO, kapolo wa Mulungu ndi mtumwi wa Yesu Kristu monga mwa cikhulupiriro ca osa nkhika a Mulungu, ndi cizindikiritso ca coonadi ciri monga mwa cipembedzo, 2 m’ciyembekezo ca moyo…
1 PAULO, kapolo wa Mulungu ndi mtumwi wa Yesu Kristu monga mwa cikhulupiriro ca osa nkhika a Mulungu, ndi cizindikiritso ca coonadi ciri monga mwa cipembedzo, 2 m’ciyembekezo ca moyo…
Maceniezedwe a okalamba ndi anyamata ndi akapolo. Akhale citsanzo yekha Tito 1 Koma iwe, lankhula zimene ziyenera ciphunzitso colamitsa: 2 okalamba akhale odzisunga, olemekezeka, odziletsa, olama m’cikhulupiriro, m’cikondi, m’cipiriro. 3…
1 Uwakumbutse iwo agonje kwa akulu, ndi aulamuliro, akhale omvera, okonzeka pa nchito iri yonse yabwino; 2 asacitire mwano munthu ali yense, asakhale andeu, akhale aulere, naonetsere cifatso conse pa…