Oweruza 11

Yefita alanditsa Israyeli 1 Yefita Mgileadi ndipo anali ngwazi yamphamvu, ndiye mwana wa mkazi wadama; koma Gileadi adabala Yefita. 2 Ndipo mkazi wa Gileadi anambalira ana amuna; koma atakula ana…

Oweruza 12

Efraimu aukira Yefita 1 Pamenepo amuna a Efraimu analalikidwa, napita kumpoto; nati kwa Yefita, Wapitiriraoji kuthira nkhondo ana a Amoni, osatiitana ife timuke nawe? Tidzakutenthera nyumba yako ndimotopamtupako. 2 Ndipo…

Oweruza 13

Aisrayeli agonjera Afilisti; abadwa Samsoni 1 Ndipo ana a Israyeli anaonjeza kucita coipa pamaso pa Yehova; nawapereka Yehova m’dzanja la Afilisti zaka makumi anai. 2 Ndipo panali munthu wina wa…

Oweruza 14

Ukwati wa Samsoni 1 Ndipo Samsoni anatsikira ku Timna, naona mkazi wa ku Timna wa ana akazi a Afilisti. 2 Nakwera iye, nauzaatatewacendi amai wace, nati, Ndapenya mkazi m’Timna wa…

Oweruza 15

Samsoni atentha za m’minda ya Afilisti 1 Ndipo kunali atapita masiku, nyengo ya kuceka tirigu Samsoni anakaceza ndi mkazi wace ndi kumtengera mbuzi, nati, Ndidzalowa kwa mkazi wanga kucipinda. Koma…

Oweruza 16

Delila apereka Samsoni 1 Ndipo Samsoni anamuka ku Gaza, naonako mkazi wadama, nalowana naye. 2 Koma wina anauza a ku Gala, ndi kuti, Samsoni walowa kuno. Pamenepo anamzinga, namlalira usiku…

Oweruza 17

Mika ndi fano lace 1 Ndipo ku mapiri a Efraimu kunali munthu dzina lace ndiye Mika. 2 Ndipo iye anati kwa amai wace, Ndarama zija mazana khumi ndi limodzi anakuberani…

Oweruza 18

Ana a Dani alanda mafano a Mika 1 Masiku ajawo panalibe mfumu m’Israyeli; masiku ajanso pfuko la Adani anadzifunira colowa cakukhalako; pakuti kufikira tsiku lija sicinawagwera colowa cao pakati pa…

Oweruza 19

Coopsa adacicita a ku Gibeya 1 Ndipo kunali, masiku aja, pamene panalibe mfumu m’Israyeli, panali munthu Mlevi wogonera kutseri kwa mapiri a Efraimu amene anadzitengera mkazi wamng’ono wa ku Betelehemu-Yuda….

Oweruza 20

Aisrayeli abwezera cilango pfuko la Benjamini 1 Pamenepo anaturuka ana onse a Israyeli, nuunjikana msonkhano kwa Yehova ku Mizipa ngati munthu mmodzi, kuyambira ku Dani mpaka Beereseba ndi dziko la…