Oweruza 1
Aisrayeli aonjeza kugonjetsa Akanani 1 NDIPO atafa Yoswa, ana a Israyeli anafunsira kwa Yehova ndi kuti, Adzayamba ndani kutikwerera pa Akanani kuwathira nkhondo? 2 Ndipo Yehova anati, Akwere Yuda; taonani,…
Aisrayeli aonjeza kugonjetsa Akanani 1 NDIPO atafa Yoswa, ana a Israyeli anafunsira kwa Yehova ndi kuti, Adzayamba ndani kutikwerera pa Akanani kuwathira nkhondo? 2 Ndipo Yehova anati, Akwere Yuda; taonani,…
Mngelo wa Mulungu adzudzula Aisrayeli 1 Ndipo mthenga wa Yehova anakwera kucokera ku Giligala kumka ku Bokimu. Ndipo anati, Ndinakukweretsani kucokera ku Aigupto, ndi kulowetsa inu m’dziko limene ndinalumbirira makolo…
Amitundu otsala akuyesa nao Aisrayeli 1 Ndipo iyo ndiyo mitundu ya anthu anaisiyapo Yehova kuyesa nayo Israyeli, ndiwo onse amene sanadziwa nkhondo zonse za Kanani; 2 cifukwa cace ndico cokha…
Debora ndi Baraki alanditsa Aisrayeli m’dzanja la Yabini 1 Ndipo ana a Israyeli anaonjeza kucita coipa pamaso pa Yehova, atafa Ehudi. 2 Ndipo Yehova anawagulitsa m’dzanja la Yabini mfumu ya…
Nyimbo ya Debora 1 Ndipo Debora ndi Baraki mwana wa Abinoamu anayimba tsiku lomwelo ndi kuti, 2 Lemekezani Yehova Pakuti atsogoleri m’Israyeli anatsogolera, Pakuti anthu anadzipereka mwaufulu. 3 Imvani mafumu…
Midyani agonjetsa Aisrayeli 1 Koma ana a Israyeli anacita coipa pamaso pa Yehova; ndipo Yehova anawapereka m’dzanja la Midyani zaka zisanu ndi ziwiri. 2 Pamene dzanja la Midyani linalaka Israyeli,…
Gideoni apitikitsa nkhondo ya Amidyani 1 Pamenepo Yerubaala, ndiye Gideoni, ndi anthu onse okhala naye anauka mamawa, namanga misasa pa citsime ca Harodi, ndi misasa ya Midyani inali kumpoto kwao,…
1 Ndipo amuna a Efraimu anati kwa iye, Ici waticitira nciani, osatiitana popita iwe kulimbana ndi Amidyani? natsutsana naye kolimba. 2 Koma ananena nao, Ndacitanji tsopano monga inu? Kodi kukunkha…
Abimeleki awapha abale ace 1 Koma Abimeleki mwana wa Yerubaala anamuka ku Sekemu kwa abale a amai wace, nanena nao, ndi kwa banja lonse la nyumba ya atate wa amai…
Tola ndi Yairi aweruza Israyeli 1 Atafa Abimeleki, anauka kupulumutsa Israyeli Tola mwana wa Puwa, mwana wa Dodo munthu wa Isakara; nakhala iye m’Sanriri ku mapiri a Efraimu. 2 Ndipo…