Nyimbo 1

Mkwatibwi anena ndi ana a Yerusalemu za mkwati 1 NYIMBO yoposa, ndiyo ya Solomo. 2 Mnyamatayo andipsompsonetse ndi m’kamwa mwace; Pakuti cikondi cako ciposa vinyo. 3 Mafuta ako anunkhira bwino;…

Nyimbo 2

1 Ndine duwa lofiira la ku Saroni, Ngakhale kakombo wa kuzigwa. 2 Ngati kakombo pakati pa minga Momwemo wokondedwa wanga pakati pa ana akazi. 3 Ngati maula pakati pa mitengo…

Nyimbo 3

Mkwatibwi apeza mkwati 1 Usiku pamphasa panga ndinamfunafuna amene moyo wanga umkonda: Ndinamfunafuna, koma osampeza. 2 Ndinati, Ndiuketu, ndiyendeyende m’mudzi, M’makwalala ndi m’mabwalo ace, Ndimfunefune amene moyo wanga umkonda: Ndimfunafuna,…

Nyimbo 4

Mkwati alemekeza mkwatibwi 1 Taona, wakongola, bwenzi langa, namwaliwe, taona, wakongola; Maso ako akunga a nkhunda patseri pa cophimba cako: Tsitsi lako likunga gulu la mbuzi, Zooneka pa phiri la…

Nyimbo 5

1 Ndalowa m’munda mwanga, mlongwanga, mkwatibwi: Ndachera nipa yanga ndi zonunkhiritsa zanga; Ndadya uci wanga ndi cisa cace; Ndamwa vinyo wanga ndi mkaka wanga. Idyani, atsamwalinu, Imwani, mwetsani cikondi. Alekana…

Nyimbo 6

1 Bwenzi lako wapita kuti, Mkaziwe woposa kukongola? Bwenzi lako wapambukira kuti, Tikamfunefune pamodzi nawe? 2 Bwenzi langa watsikira kumunda kwace, Ku zitipula za mphoka, Kukadya kumunda kwace, ndi kuchera…

Nyimbo 7

1 Ha, mapazi ako akongola m’zikwakwata, Mwana wamkaziwe wa mfumu! Pozinga m’cuuno mwako pakunga zonyezimira, Nchito ya manja a mmisiri waluso. 2 Pamcombo pako pakunga cikho coulungika, Cosasowamo vinyo wosanganika:…

Nyimbo 8

1 Mwenzi utakhala ngati mlongwanga, Woyamwa pa bere la amai! Ndikadakupeza panja, ndikadakupsompsona; Osandinyoza munthu. 2 Ndikadakutsogolera, kukulowetsa m’nyumba ya amai, Kuti andilange mwambo; Ndikadakumwetsa vinyo wokoleretsa, Ndi madzi a…