Numeri 31

Aisrayeli agonjetsa Amidyani 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Abwezereni cilango Amidyani cifukwa ca ana a Israyeli; utatero udzaitanidwa kumka kwa anthu a mtundu wako. 3 Ndipo Mose…

Numeri 32

Arubeni, Agadi, ndi Amanase alandira colowa cao tsidya lino la Yordano 1 Koma ana a Rubeni ndi ana a Gadi anali nazo zoweta zambirimbiri; ndipo anapenyerera dziko la Yazeri, ndi…

Numeri 33

Za ulendo wa Aisrayeli pakati pa Ramese ndi Sitimu 1 Maulendo a ana a Israyeli amene anaturuka m’dziko la Aigupto monga mwa makamu ao, ndi dzanja la Mose ndi Aroni,…

Numeri 34

Malire a dziko la Kanani 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Uza ana Israyeli, nunene nao, Mutalowa a m’dziko la Kanani, ndilo dziko logwera inu, likhale colowa canu,…

Numeri 35

Midzi ya Alevi 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose m’zidikha za Moabu, pa Yordano, ku Yeriko, ndi kuti, 2 Uza ana a Israyeli, kuti apatseko Alevi colowa cao cao, midzi…

Numeri 36

Za kukwatibwa kwa ana akazi olandira colowa 1 Ndipo akuru a makolo a mabanja a ana a Gileadi, mwana wa Makiri, mwana wa Manase, wa mabanja a ana a Yosefe,…