Numeri 11
Kudandaula kwa Aisrayeli 1 Ndipo anthu anaipa, namadandaula m’makutu a Yehova; ndipo pamene Yehova anamva anapsa mtima; ndi mota wa Yehova unayaka pakati pao, nunyeketsa ku cilekezero ca cigono. 2…
Kudandaula kwa Aisrayeli 1 Ndipo anthu anaipa, namadandaula m’makutu a Yehova; ndipo pamene Yehova anamva anapsa mtima; ndi mota wa Yehova unayaka pakati pao, nunyeketsa ku cilekezero ca cigono. 2…
Miriamu ndi Aroni aukira Mose 1 Ndipo Miriamu ndi Aroni anatsutsana naye Mose cifukwa ca mkazi mtundu wace Mkusi amene adamtenga; popeza adatenga mkazi Mkusi. 2 Ndipo anati, Kodi Yehova…
Atumidwa amuna 12 kukazonda Kanani 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Udzitumire amuna, kuti azonde dziko la Kanani, limene ndirikupatsa ana a Israyeli; utumize munthu mmodzi wa pfuko…
Aisrayeli afuna kubwerera kumka ku Aigupto 1 Pamenepo khamu lonse linakweza mau ao, napfuula; ndipo anthuwo analira usikuwo. 2 Ndipo ana onse a Israyeli anadandaulira Mose ndi Aroni; ndi khamu…
Malamulo a pa nsembezo 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose nati, 2 Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Mukakalowa m’dziko lokakhalamo inu, limene ndirikupatsa inu, 3 ndipo mukakonzera Yehova…
Kora, Datani, ndi Abiramu aukira Mose 1 Koma Kora, mwana wa Izara, mwana wa Kohati, mwana wa Levi, anatenga Datani ndi Abiramu, ana a Eliyabu, ndi Oni mwana wa Peleti,…
Ndodo ya Aroni iphuka 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Nena ndi ana a Israyeli, nulandire kwa yense ndodo, banja liri onse la makolo ndodo imodzi, mafuko ao…
Udindo wa ansembe ndi Alevi, ndi zolandira zao 1 Ndipo Yehova anati kwa Aroni, Iwe ndi ana ako amuna ndi banja la kholo lako pamodzi ndi iwe muzisenza mphulupulu ya…
Za ng’ombe yamsoti yofiira ndi madzi oyeretsa nao 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati, 2 Ili ndi lemba la cilamulo Yehova adalamuliraci, ndi kuti, Nena ndi ana…
Imfa ya Miriamu; madzi a Meriba 1 Ndipo ana a Israyeli, ndilo khamu lonse, analowa m’cipululu ca Zini mwezi woyamba; ndipo anthu anakhala m’Kadesi; kumeneko anafa Miriamu, naikidwakomweko. 2 Ndipo…