Numeri 1
Aisrayeli awerengedwa m’cipululu ca Sinai 1 NDIPO Yehova ananena ndi Mose m’cipululu ca Sinai, m’cihema cokomanako, tsiku loyamba la mwezi waciwiri, caka caciwiri ataturuka m’dziko la Aigupto, ndi kuti, 2…
Aisrayeli awerengedwa m’cipululu ca Sinai 1 NDIPO Yehova ananena ndi Mose m’cipululu ca Sinai, m’cihema cokomanako, tsiku loyamba la mwezi waciwiri, caka caciwiri ataturuka m’dziko la Aigupto, ndi kuti, 2…
Malongosoledwe a cigono 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati, 2 Ana a Israyeli azimanga mahema ao yense ku mbendera yace, ya cizindikilo ca nyumba ya kholo lace;…
Nchito ya Alevi 1 Mibadwo ya Aroni ndi Mose, tsiku lija Yehova ananena ndi Mose m’phiri la Sinai, ndi iyo. 2 Ndipo maina ao a ana amuna a Aroni ndi…
Akohati 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati, 2 Werengani ana a Kohati pakati pa ana a Levi, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao,…
Odetsedwa onse acotsedwe kucigono 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Uza ana a Israyeli kuti aziturutsa m’cigono akhate onse, ndi onse akukhala nako kukha, ndi onse odetsedwa…
Za cowinda ca Mnaziri 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Mwamuna kapena mkazi akadzipatulira kulonieza cowinda ca Mnaziri, kudzipatulira kwa Yehova;…
Zopereka za Akuru 12 atautsa cihemaco 1 Ndipo kunali kuti tsiku lomwe Mose anatsiriza kumuutsa kacisi, namdzoza ndi kumpatula, ndi zipangizo zace zonse, ndi guwa la nsembe, ndi zipangizo zace…
Za kuyatsa nyalizo 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Nena kwa Aroni, nuti naye, Pamene uyatsa nyalizo, nyali manu ndi ziwirizo ziwale pandunji pace pa coikapo nyalico. 3…
Acita Paskha 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose m’cipululu ca Sinai, mwezi woyamba wa caka caciwiri ataturuka m’dziko la Aigupto, ndi kuti, 2 Ana a Israyeli acite Paskha pa nyengo…
Adzipangira malipenga awiri asiliva 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Dzipangire malipenga awiri asiliva; uwasule mapangidwe ace; ucite nao poitana khamu, ndi poyendetsa a m’zigono. 3 Akaliza, khamu…