Nehemiya 1
Nehemiya apempherera ana a lsrayeli kwa Mulungu 1 MAU a Nehemiya mwana wa Hakaliya. Kunali tsono mwezi wa Kisilevi, caka ca makumi awiri, pokhala ine ku Susani ku nyumba ya…
Nehemiya apempherera ana a lsrayeli kwa Mulungu 1 MAU a Nehemiya mwana wa Hakaliya. Kunali tsono mwezi wa Kisilevi, caka ca makumi awiri, pokhala ine ku Susani ku nyumba ya…
Aritasasta alola Nehemiya akamange linga la Yerusalemu 1 Koma kunacitika mwezi wa Nisana, caka ca makumi awiri ca Aritasasta mfumu pokhala vinyo pamaso pace, ndinatenga vinyoyo ndi kuipatsa mfumu. Koma…
Mamangidwe a malinga ndi zipata za Yerusalemu 1 Pamenepo Eliasibu mkuru wa ansembe ananyamuka pamodzi ndi abale ace ansembe, namanga cipata cankhosa; anacipatula, naika zitseko zace, inde anacipatula mpaka nsanja…
Adani ayesa kuwaletsa kumanga malinga 1 Ndipo kunali, atamva Sanibalati kuti tinalikumanga lingali, kudamuipira, nakwiya kwakukuru, naseka Ayuda pwepwete. 2 Nanena iye pamaso pa abale ace ndi ankhondo a ku…
Nehemiya acinjiriza aumphawi opsinjika 1 Pamenepo panamveka kulira kwakukuru kwa anthu ndi akazi ao kudandaula pa abale ao Ayuda. 2 Popeza panali ena akuti, Ife, ana athu amuna ndi akazi,…
Adani ayesa kunyenga ndi kuopsa Nehemiya 1 Kunali tsono, atamva Sanibalati, ndi Tobiya, ndi Gesemu M-arabu, ndi adani athu otsala, kuti ndidatha kumanga lingali, posatsalaponso popasuka; (ngakhale pajapo sindinaika zitseko…
Alonda adikira Yerusalemu 1 Ndipo atatha kumanga linga, ndinaika zitseko, nakhazika odikira, ndi oyimbira, ndi Alevi; 2 ndipo ndinawapatsa mbale wanga Hanani, ndi Hananiya kazembe wa kuboma, ulamuliro wa pa…
Ezara awerengera anthu buku la cilamulo 1 Ndipo anthu onse anasonkhana ngati munthu mmodzi ku khwalala liri ku cipata ca kumadzi, namuuza Ezara mlembi atenge buku la cilamulo ca Mose,…
Msonkhano wa kusala ndi kupemphera 1 Ndipo tsiku la makumi awiri mphambu anai la mwezi uno ana a Israyeli anasonkhana ndi kusala, ndi kubvala ciguduli, ndipo anali ndi pfumbi. 2…
Pangano lokhazikika pakati pa anthu ndi Mulungu 1 Okomera cizindikilo tsono ndiwo Nehemiya, Tirisata mwana wa Hakaliya, ndi Zedekiya, 2 Seraya, Agariya, Yeremiya, 3 Pasuri, Amariya, Malikiya, 4 Hatusi, Sebaniya,…