Mlaliki 1

Za pansi pano nzacabe 1 MAU a Mlaliki, mwana wa Davide, mfumu ya m’Yerusalemu. 2 Zacabecabe, ati Mlaliki; zacabecabe zonse ndi cabe. 3 Kodi nchito zace zonse munthu asauka nazo…

Mlaliki 2

Za m’moyo uno sizitha kukondweretsa mtima 1 Ndinati mumtima mwanga, Tiyetu, ndikuyese ndi cimwemwe; tapenya tsono zabwino; ndipo taona, icinso ndi cabe. 2 Ndinati, Kuseka ndi misala; ndi cimwemwe kodi…

Mlaliki 3

Ziri zofise ziri ndi nyengo yace, Mulungu ndi kuziika zonse 1 Kanthu kali konse kali ndi nthawi yace ndi cofuna ciri conse ca pansi pa thambo ciri ndi mphindi yace;…

Mlaliki 4

Matsoka ndi mabvuto a moyo uno 1 Ndinabweranso tsono ndi kupenyera nsautso zonse zimacitidwa kunja kuno; ndipo taona, misozi ya otsenderezedwa, koma analibe wakuwatonthoza; ndipo akuwatsendereza anali ndi mphamvu koma…

Mlaliki 5

Malangizo osiyana akuwasamalira anthu m’moyo uno 1 Samalira phazi lako popita ku nyumba ya Mulungu; pakuti kuyandikira kumvera kupambana kupereka nsembe za zitsiru; pakuti sizizindikira kuti zirikucimwa. 2 Usalankhule mwanthuku…

Mlaliki 6

Ngakhale Mulungu apatsa munthu zonse azikhumba koma mtima sukhuta nazo 1 Pali coipa ndaciona kunja kuno cifalikira mwa anthu, 2 munthu amene Mulungu wamlemeretsa nampatsa cuma ndi ulemu, mtima wace…

Mlaliki 7

Kumva zowawa nkokoma, nzeru ndi kudziletsa momwemo 1 Mbiri yabwino iposa zonunkhira zabwino; ndi tsiku lakumwalira liposa tsiku lakubadwa. 2 Kunka ku nyumba ya maliro kupambana kunka ku nyumba ya…

Mlaliki 8

Langizo la kumvera mfumu 1 Ndani akunga wanzeru? Ndani adziwa tanthauzo la mau? Nzeru ya munthu iwalitsa nkhope yace, kuduwa kwa nkhope yace ndi kusanduka. 2 Nditi, Sunga mau a…

Mlaliki 9

Okoma ndi oipa amamva zomwezo. Khalani nazo zakupatsa Mulungu mokondwera 1 Pakuti zonsezi ndinazisunga mumtima ndikalondoletu zonsezi; kuti olungama ndi anzeru ndi nchito zao ali m’manja a Mulungu; ngakhale kukonda…

Mlaliki 10

Kupusa kusautsa kwambiri 1 Nchenche zakufa zinunkhitsa moipa nizioletsa mafuta onunkhira a sing’anga; comweco kupusa kwapang’ono kuipitsa iye amene achuka cifukwa ca nzeru ndi ulemu. 2 Wanzeru, mtima wace uli…