Miyambi 21
1 Mtima wa mfumu uli m’dzanja la Yehova ngati mitsinje ya madzi; Aulozetsa komwe afuna. 2 Njira zonse za munthu zilungama pamaso pace; Koma Yehova ayesa mitima. 3 Kucita cilungamo…
1 Mtima wa mfumu uli m’dzanja la Yehova ngati mitsinje ya madzi; Aulozetsa komwe afuna. 2 Njira zonse za munthu zilungama pamaso pace; Koma Yehova ayesa mitima. 3 Kucita cilungamo…
1 Mbiri yabwino ifunika kopambana cuma cambiri; Kukukomera mtima anzako kuposa siliva ndi golidi. 2 Wolemera ndi wosauka akumana, Wolenga onsewo ndiye Yehova. 3 Wocenjera aona zoipa, nabisala; Koma acibwana…
1 Pamene ukhala ulinkudya ndi mkuru, Zikumbukira ameneyo ali pamaso pako; 2 Nuike mpeni pakhosi pako, Ngati uli wadyera. 3 Usakhumbe zolongosoka zace; Pokhala zakudya zonyenga. 4 Usadzitopetse kuti ulemere;…
1 Usacitire nsanje anthu oipa, Ngakhale kufuna kukhala nao; 2 Pakuti mtima wao ulingalira za cionongeko; Milomo yao ilankhula za mphulupulu. 3 Nzeru imangitsa nyumba; Luntha liikhazikitsa. 4 Kudziwa kudzaza…
Miyambo ya Solomo yosonkhanitsa nthawi ya Hezekiya 1 Iyinso ndiyo miyambo ya Solomo Imene anthu a Hezekiya mfumu ya Yuda anailemba. 2 Kubisa kanthu ndi ulemerero wa Mulungu; Koma ulemerero…
1 Monga cipale cofewa m’malimwe, ndi mvula m’masika, Momwemo ulemu suyenera citsiru. 2 Monga mpheta irikuzungulira, ndi namzeze alikuuluka, Momwemo temberero la pacabe silifikira. 3 Cikoti ciyenera kavalo, ndi cam’kamwa…
1 Usanyadire zamawa, Popeza sudziwa tsiku lina lidzabala ciani? 2 Wina akutame, si m’kamwamwako ai; Mlendo, si milomo ya iwe wekha. 3 Mwala ulemera, mcenga ndiwo katundu; Koma mkwiyo wa…
Mau olinganiza zosiyana 1 Woipaathawapalibewomthamangitsa; Koma olungama alimba mtima ngati mkango. 2 Pocimwa dziko akalonga ace acuruka; Koma anthu ozindikira ndi odziwa alikhazikikitsa nthawi yaikuru. 3 Munthu waumphawi wotsendereza osauka…
1 Yemwe aumitsa khosi atadzudzulidwa kwambiri, Adzasweka modzidzimuka, palibe comciritsa. 2 Pocuruka olungama anthu akondwa; Koma polamulira woipa anthu ausa moyo. 3 Mwamuna wokonda nzeru akondweretsa atate wace; Koma wotsagana…
Cibvomerezo, pemphero ndi malangizo a Aguri 1 Mau a Aguri mwana wa Yake; uthenga. Munthuyo anati, Ndadzitopetsa, Mulungu; Ndadzitopetsa, Mulungu, ndathedwa; 2 Pakuti ndipambana anthu onse kupulukira, Ndiribe luntha la…