Miyambi 1
Zocitira miyambi 1 MIYAMBI ya Solomo mwana wa Davide, mfumu ya Israyeli. 2 Kudziwa nzeru ndi mwambo; Kuzindikira mau ozindikiritsa; 3 Kulandira mwambo wakusamalira macitidwe, Cilungamo, ciweruzo ndi zolunjika; 4…
Zocitira miyambi 1 MIYAMBI ya Solomo mwana wa Davide, mfumu ya Israyeli. 2 Kudziwa nzeru ndi mwambo; Kuzindikira mau ozindikiritsa; 3 Kulandira mwambo wakusamalira macitidwe, Cilungamo, ciweruzo ndi zolunjika; 4…
Ukoma ndi phindu tace la Nzeru 1 Mwananga, ukalandira mau anga, Ndi kusunga malamulo anga; 2 Kucherera makutu ako kunzeru, Kulozetsa mtima wako kukuzindikira; 3 Ukaitananso luntha, Ndi kupfuulira kuti…
Malangizo a kuopa, kukhulupira, ndi kumvera Yehova 1 Mwananga, usaiwale malamulo anga, Mtima wako usunge malangizo anga; 2 Pakuti adzakuonjezera masiku ambiri, Ndi zaka za moyo ndi mtendere. 3 Cifundo…
Ceniezo lakuti afune Nzeru nalewe njira za oipa 1 Ananu, mverani mwambo wa atate, Nimuchere makutu mukadziwe luntha; 2 Pakuti ndikuphunzitsani zabwino; Musasiye cilangizo canga. 3 Pakuti ndinali mwana kwa…
Acenjere naye mkazi woipa 1 Mwananga, mvera nzeru yanga; Cherera makutu ku luntha langa; 2 Ukasunge zolingalira, Milomo yako ilabadire zomwe udziwa. 3 Pakuti milomo ya mkazi waciwerewere ikukha uci;…
Za kuperekera mnzace cikole. Zisanu ndi ziwiri zoipira Mulungu 1 Mwananga, ngati waperekera mnzako cikole, Ngati wapangana kulipirira mlendo, 2 Wakodwa ndi mau a m’kamwa mwako, Wagwidwa ndi mau a…
Acenjere naye mkazi woipa 1 Mwananga, sunga mau anga, Ukundike malangizo anga; 2 Sunga malangizo anga, nukhale ndi moyo; Ndi malamulo anga ngati mwana wa diso lako. 3 Uwamange pa…
Nzeru ipambana m’kucita kwace 1 Kodi nzeru siitana, Luntha ndi kukweza mau ace? 2 Iima pamwamba pa mtunda, Pa mphambano za makwalala; 3 Pambali pa cipata polowera m’mudzi, Polowa anthu…
Madyerero a Nzeru 1 Nzeru yamanga nyumba yace, Yasema zoimiritsa zace zisanu ndi ziwiri; 2 Yaphera nyama yace, nisanganiza vinyo wace, Nilongosolanso pa gome lace. 3 Yatuma anamwali ace, iitana…
Miyambo yosiyana-siyana; Miyambo ya Sotomo 1 Mwana wanzeru akondweretsa atate; Koma mwana wopusa amvetsa amace cisoni. 2 Cuma ca ucimo sicithangata: Koma cilungamo cipulumutsa kuimfa. 3 Yehova samvetsa njala moyo…