Masalmo 81

Mulungu atonza Aisrayeli pa kusamvera kwao Kwa mkulu wa Nyimbo, pa Giliti. Salmo la Asafu. 1 Yimbitsirani Mulungu ndiye mphamvu yathu; Pfuulirani kwa Mulungu wa Yakobo. 2 Utsani Salimo, bwera…

Masalmo 82

Oweruza aweruze bwino Salmo la Asatu. 1 Mulungu aima mu msonkhano wa Mulungu, Aweruza pakati pa milungu. 2 Mudzaweruza mosalunjika kufikira liti, Ndi kusamalira nkhope ya oipa? 3 Weruzani osauka…

Masalmo 83

Amitundu apangana kuononga Aisrayeli, Apempha Mulungu awalanditse Nyimbo. Satmo la Asatu. 1 Mulungu musakhale cete; Musakhale du, osanena kanthu, Mulungu. 2 Pakuti taonani, adani anu aphokosera: Ndipo okwiyira Inu aweramutsa…

Masalmo 84

Okhala m’nyumba ya Yehova ndiwo amwai Kwa Mkulu wa Nyimbo, pa Gitili: Salmo la ana a Kora. 1 Pokhala Inu mpotikonda ndithu, Yehova wa makamu! 2 Moyo wanga ulakalaka, inde…

Masalmo 85

Akumbutsa Mulungu madalitso akale, apempha awabwereze Kwa Mkulu wa Nyimbo: Satmo la ana a Kora. 1 Munacita zobvomereza dziko lanu, Yehova; Munabweza ukapolo wa Yakobo. 2 Munacotsa mphulupulu ya anthu…

Masalmo 86

Davide apempha Mulungu kolimba amlanditse Pemphero la Davide. 1 Cherani khutu lanu Yehova, mundiyankhe; Pakuti ine ndine wozunzika ndi waumphawi. 2 Sungani moyo wanga pakuti ine ndine wokondedwa wanu; Inu…

Masalmo 87

Yehova akonda Ziyoni Salmo la ana a Kora: Nyimbo. 1 Maziko ace ali m’mapiri oyera. 2 Yehova akonda zipata za Ziyoni Koposa zokhalamo zonse za Yakobo. 3 Mudzi wa Mulungu,…

Masalmo 88

Wa Salmo achula masautso ace, napempha Mulungu amdalitse kuimfa Nyimbo. Salmo la ana a Kora. Kwa Mkulu wa Nyimbo, pa Mahalata Leanotu. Cilangizo ca Hemana M-ezara. 1 Yehova, Mulungu wa…

Masalmo 89

Pangano la Mulungu ndi Davide. Mulungu adzapulumutsa anthu ace Cilangizo ca Etana M-ezera. 1 Ndidzayimbira zacifundo za Yehova nthawi yonse: Pakamwa panga ndidzadziwitsira cikhulupiriko canu ku mibadwo mibadwo. 2 Pakuti…

Masalmo 90

Mulungu ndiye wacikhalire, munthu ndiye wakutha msanga Pemphero la Mose munthu wa Mulungu. 1 Ambuye, Inu munatikhalira mokhalamo M’mibadwo mibadwo. 2 Asanabadwe mapiri, Kapena musanalenge dziko lapansi, ndi lokhalamo anthu,…