Masalmo 71

Nkhalamba idziponya kwa Mulungu amene anamkhulupira kuyambira ubwana wace 1 Ndikhulupirira Inu, Yehova: Ndisacite manyazi nthawi zonse. 2 Ndikwatuleni m’cilungamo canu, ndi kundilanditsa: Ndicherereni khutu lanu ndi kundipulumutsa. 3 Mundikhalire…

Masalmo 72

Za ufumu wa Mfumu yokoma Salimo la kwa Solomo. 1 Patsani mfumu maweruzo anu, Mulungu, Ndi mwana wa mfumu cilungamo canu. 2 Potero adzanenera anthu anu mlandu ndi m’cilungamo, Ndi…

Masalmo 73

Kupindula kwa oipa kumakayikitsa pa cilungamo ca Mulungu, koma citsiriziro cao citibvomerezetsa cilungamoco Salimo la Asafu. 1 Indedi Mulungu acitira Israyeli zabwino, Iwo a mtima wa mbe. 2 Koma ine,…

Masalmo 74

Malo oyera adetsedwa. Apempha Mulungu akumbuke cipangano cao Cilangizo ca Asaru. 1 Mulungu, munatitayiranji citayire? Mkwiyo wanu ufukiranji pa nkhosa za kubusa kwanu? 2 Kumbukilani msonkhano wanu, umene munaugula kale,…

Masalmo 75

Mulungu woweruza asiyanitsa pakati pa odzikuza ndi olungama Kwa Mkulu wa Nyimbo: Altasayeti: Salmo la Asafu. Nyimbo. 1 Tikuyamikani Inu, Mulungu; Tiyamika, pakuti dzina lanu liri pafupi; Afotokozera zodabwiza zanu,…

Masalmo 76

Ulemerero ndi mphamvu ya Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo: pa Negtnolo. Salmo la Asafu. Nyimbo. 1 Mulungu adziwika mwa Yuda: Dzina lace limveka mwa Israyeli. 2 Msasa wace unali m’Salemu,…

Masalmo 77

Acitankhawapokumbuka zocita Mulungu, koma alimbika mtima pokumbuka zina adazicita Iye Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Yedutunu; Salmo la Asaru. 1 Ndidzapfuulira kwa Mulungu ndi mau anga; Kwa Mulungu ndi mau…

Masalmo 78

Cikondi ndi cipiriro ca’Mulungu ca pa Aisrayeli osakhulupirika Cilangizo ca Asatu. 1 Tamverani, anthu anga, cilamulo canga; Cherezani khutu lanu mau a pakamwa panga. 2 Ndidzatsegula pakamwa panga mofanizira; Ndidzachula…

Masalmo 79

Yerusalemu apasuka, apempha Mulungu awathandize Salmo la Asafu. 1 Mulungu, akunja alowa m’colandira canu; Anaipsa Kacisi wanu woyera; Anacititsa Yerusalemu bwinja. 2 Anapereka mitembo ya atumiki anu ikhale cakudya ca…

Masalmo 80

Apempha Mulungu alanditse anthu ace m’cisautso cao Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Svosvantmuj locita mboni; Salmo la Asafu. 1 Mbusa wa Israyeli, cherani khutu; Inu wakutsogolera Yosefe ngati nkhosa; Inu…