Masalmo 41
Mulungu adalitsa wosamalira osauka. Adani ndi mabwenzi amcitira Davide zoipa, Mulungu amlanditse Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide. 1 Wodala iye amene asamalira wosauka: Tsiku la tsoka Yehova adzampulumutsa:…
Mulungu adalitsa wosamalira osauka. Adani ndi mabwenzi amcitira Davide zoipa, Mulungu amlanditse Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide. 1 Wodala iye amene asamalira wosauka: Tsiku la tsoka Yehova adzampulumutsa:…
Mtima wolira kuyanjana ndi Mulungu m’Kacisi Kwa Mkulu wa Nyimbo. Cilangizo ca kwa ana a Kora. 1 Monga nswala ipuma wefuwefu kukhumba mitsinje; Motero moyo wanga upuma wefuwefu kukhumba Inu,…
Davide alira akhale ku Kacisi 1 Mundiweruzire, Mulungu, ndipo mundinenere mlandu kwa anthu opanda cifundo: Mundilanditse kwa munthu wonyenga ndi wosalungama. 2 Pakuti Inu ndinu Mulungu wa mphamvu yanga; mwanditayiranji?…
Anthu a Mulungu akumbuke zithandizo zakale popempha cipulumutso m’tsoka lao Kwa Mkulu Wa Nyimbo; Cuangizo ca ana a Kora. 1 Mulungu, tidamva m’makutu mwathu, makolo athu anatisimbira, Za nchitoyo mudaicita…
Nyimbo voyimbira ukwati wa mfumu Kwa Mkulu wa Nyimbo pa Syosyanim. Cilangizo ca kwa ana a Kora. Nyimbo ya cikondi. 1 Mtima wanga usefukira naco cinthu cokoma: Ndinena zopeka ine…
Mulungu ndiye pothawirapo anthu ace Kwa Mkulu wa Nyimbo; Cilangizo ca kwa ana a Kora. Pa Alamot. Nyimbo. 1 Mulungu ndiye pothawirapo pathu ndi mphamvu yathu, Thandizo lopezekeratu m’masautso. 2…
Mau a kulemekeza Mulungu mwini dziko lonse lapansi Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la ana a Koro. 1 Ombani m’manja, mitundu yonse ya anthu; Pfuulirani kwa Mulungu ndi liu la…
Ukoma ndi ulemerero wa Ziyoni Nyimbo; Salmo la ana a Kora. 1 Yehova ndiye wamkulu, ayenera kulemekezekadi, M’mudzi wa Mulungu wathu, m’phiri lace loyera. 2 Phiri la Ziyoni, cikhalidwe cace…
Za pansi pano nza cabe Kwa Mkulu wa Nyimbo; Salmo la ana a Kora. 1 Dzamveni kuno, anthu inu nonse; Cherani khutu, inu nonse amakono, 2 Awamba ndi omveka omwe,…
Mulungu woweruza wa dziko lapansi Salmo la Asafu. 1 Mulungu wa milungu, Yehova, wanena, Aitana dziko lapansi kuyambira kuturuka kwa dzuwa kufikira kulowa kwace. 2 Mulungu awalira m’Ziyoni, mokongola mwangwiro….