Masalmo 31
Davide apempha kolimba Mulungu amlanditse, natama cifundo cao, nauzitsa anthu a Mulungu amtame Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide. 1 Ndakhulupirira Inu, Yehova, ndikhale wopanda manyazi nthawi zonse: Mwa…
Davide apempha kolimba Mulungu amlanditse, natama cifundo cao, nauzitsa anthu a Mulungu amtame Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide. 1 Ndakhulupirira Inu, Yehova, ndikhale wopanda manyazi nthawi zonse: Mwa…
Mwai wa munthu amene Mulungu wamkhululukira Cilangizo ca Davide. 1 Wodala munthuyo wokhululukidwa chimo lace; Wokwiriridwa coipa cace. 2 Wodala munthuyu Yehova samwerengera mphulupulu zace; Ndimo mumzimu mwace mulibe cinyengo….
Alemekeza Mulungu wolenga, wosunga zonse 1 Pfuulani mokondwera mwa Yehova, inu olungama mtima: Oongoka mtima ayenera kulemekeza. 2 Yamikani Yehova ndi zeze: Myimbireni ndi cisakasa ca zingwe khumi. 3 Mumyimbire…
Davide alemekeza Yehova womlanditsa, nafulumiza ena amtame Salimo la Davide. Muja anasintha makhalidwe ace pamaso pa Abimeleke, amene anampitikitsa ndipo anacoka. 1 Ndidzalemekeza Yehova nyengo zonse; Kumlemekeza kwace kudzakhala m’kamwa…
Davide apempha Mulungu alange otpa Salmo la Davide, 1 Tsutsanani nao iwo akutsutsana nane, Yehova: Limbanani nao iwo akulimbana nane. 2 Gwirani cikopa cocinjiriza, Ukani kundithandiza. 3 Sololani nthungo, ndipo…
Kuipitsitsa kwa anthu, kukometsetsa kwa Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salimo la Davide, mtumiki wa Yehova. 1 Colakwa ca woipayo cimati m’kati mwa mtima wanga, Palibe kuopa Mulungu pamaso pace….
Kusangalala kwa ocimwa kudzatha, olungama akhalitsa nathandizidwa ndi Mulungu Salmo la Davide. 1 Usabvutike mtima cifukwa ca ocita zoipa, Usacite nsanje cifukwa ca ocita cosalungama. 2 Pakuti adzawamweta msanga monga…
Davide aulula zoipa zace, apempha Mulungu amkhululukire namthandize Salmo la Davtde, lakukumbutsa. 1 Yehova, musandidzudzule ndi mkwiyo wanu: Ndipo musandilange moopsa m’mtima mwanu. 2 Pakuti mibvi yanu yandilowa, Ndi dzanja…
Kupepuka kwa moyo uno Kwa Mkulu wa Nyimbo, kwa Yedutun, Salmo la Davide. 1 Ndinati, Ndidzasunga njira zanga, Kuti ndingacimwe ndi lilime langa: Ndidzasunga pakamwa panga ndi cam’kamwa, Pokhala woipa…
Alemekeza cipulumutso ca Mulungu, alalikira poyera cilungamo ca Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salmo la Davide. 1 Kuyembekeza ndayembekeza Yehova; Ndipo anandilola, namva kupfuula kwanga. 2 Ndipo anandikweza kunditurutsa m’dzenje…