Masalmo 21

Davide ayamika Mulungu pa kugonjetsa adani Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salimo la Davide, 1 Yehova, adzasekera mfumu mu mphamvu yanu; Adzakondwera kwakukuru m’cipulumutso canu! 2 Mwampatsa iye cikhumbo ca mtimawace,…

Masalmo 22

Posautsidwa Davide adandaulira, apemphera, ayamika Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Ajelet Hasakara, Salmo la Davide. 1 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine? Mukhaliranji kutali kwa cipulumutso canga, ndi kwa…

Masalmo 23

Amwai amene Yehova akhala Mbusa wao Salimo la Davide, 1 Yehova ndiye mbusa wanga; sindidzasowa. 2 Andigonetsa ku busa lamsipu: Anditsogolera ku madzi ndikha. 3 Atsitsimutsa moyo wanga; Anditsogolera m’mabande…

Masalmo 24

Ulemerero wa Yehova Salmo la Davide, 1 Dziko lapansi nla Yehova ndi zodzala zace zomwe, Dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhala m’mwemo. 2 Pakuti Iye analimanga pazinyanja, Nalikhazika pamadzi. 3…

Masalmo 25

Davide apempha Mulungu amlanditse kwa adani Salmo la Davide. 1 Ndikweza moyo wanga kwa Inu, Yehova. 2 Mulungu wanga, ndakhulupirira Inu, Ndisacite manyazi; Adani anga asandiseke ine. 3 Inde, onse…

Masalmo 26

Davide popempha Mulungu amweruze, achula zokoma zace Salmo la Davide. 1 Mundiweruze, Yehova, pakuti ndayenda m’ungwiro wanga: Ndipo ndakhulupirira Yehova, sindidzaterereka. 2 Mundiyesere, Yehova, ndipo mundisunthe; Yeretsani imso zanga ndi…

Masalmo 27

Davide atamadi Yehova, naliradi kuyanjana ndi Mulungu Salmo la Davide, 1 Yehova ndiye kuunika kwanga ndi cipulumutso canga; ndidzaopa yani? Yehova ndiye mphamvu ya moyo wanga; ndidzacita mantha ndi yani?…

Masalmo 28

Apempha cipulumutso, ayamika populumutsidwa Salmo la Davide. 1 Kwa Inu, Yehova, ndidzapfuulira; Thanthwe langa, musandikhalire ngati wosamva: Pakuti ngati munditontholera ine, Ndidzafanana nao iwo akutsikira kumanda. 2 Mverani mau a…

Masalmo 29

Acenjeza akuru alemekeze Mulungu Salmo la Davide. 1 Perekani kwa Yehova, inu ana a amphamvu, Perekani kwa Yehova ulemerero ndi mphamvu. 2 Perekani kwa Yehova ulemerero wa dzina lace: Gwadirani…

Masalmo 30

Mkwiyo wa Mulungu ukhala kanthawi, kuyanja kwao ndi kosatha Salmo la Davide. Nyimbo yakuperekera nyumba kwa Mulungu. 1 Ndidzakukwezani, Yehova; pakuti mwandinyamutsa, Ndipo simunandikondwetsera adani anga, 2 Yehova, Mulungu wanga,…