Masalmo 131
Kudzicepetsa kwa Davide pakupemphera Nyimbo yokwerera, ya Davide. 1 Yehova, mtima wanga sunadzikuza Ndi maso anga sanakwezeka; Ndipo sindinatsata zazikuru, Kapena zodabwiza zondiposa. 2 Indedi, ndinalinganiza ndi kutontholetsa moyo wanga;…