Masalmo 121

Mulungu Msungi wokhulupirika wa anthu ace Nyimbo yokwerera. 1 Ndikweza maso anga kumapiri: Thandizo langa lidzera kuti? 2 Thandizo langa lidzera kwa Yehova, Wakulenga zakumwamba ndi dziko lapansi. 3 Sadzalola…

Masalmo 122

Apempherera mtendere wa Yerusalemu Nyimbo yokwerera: ya Davide. 1 Ndinakondwera m’mene ananena nane, Tiyeni ku nyumba ya Yehova. 2 Mapazi athu alinkuima M’zipata zanu, Yerusalemu. 3 Yerusalemu anamangidwa Ngati mudzi…

Masalmo 123

Pemphero la wonyozedwa Nyimbo yokwerera. 1 Ndikweza maso anga kwa Inu, Kwa Inu wakukhala kumwamba. 2 Taonani, monga maso a anyamata ayang’anira dzanja la ambuye ao, Monga maso a adzakazi…

Masalmo 124

Mulungu yekha walanditsa anthu ace Nyimbo vokwerera: ya Davide, 1 Akadapanda kukhala nafe Yehova, Anene tsono Israyeli; 2 Akadapanda kukhala nafe Yehova, Pakutiukira anthu: 3 Akadatimeza amoyo, Potipsera mtima wao….

Masalmo 125

Okhulupirira Yehova akhazikika mtima Nyimbo yokwerera. 1 Iwo akukhulupirira Yehova Akunga phiri la Ziyoni, losasunthika, likhazikika kosatha, 2 Monga mapiri azinga Yerusalemu, Momwemo Yehova azinga anthu ace, Kuyambira tsopano kufikira…

Masalmo 126

Ayamikira mokondwerera kuti Mulungu anabweza ukapolo wao Nyimbo yokwerera. 1 Pobweza Yehova ukapolo wa Ziyoni, Tinakhala ngati anthu akulota. 2 Pamenepo pakamwa pathu panadzala ndi kuseka, Ndi lilime lathu linapfuula…

Masalmo 127

Madalitso onse, a m’banja omwe, acokera kwa Mulungu Nyimbo vokwerera; ya Solomo. 1 Akapanda kumanga nyumba Yehova, Akuimanga agwiritsa nchito cabe; Akapanda kusunga mudzi Yehoya, Mlonda adikira cabe. 2 Kuli…

Masalmo 128

Wakuopa Yehova adalitsidwa m’banja mwace Nyimbo yokwerera. 1 Wodala yense wakuopa Yehova, Wakuyenda m’njira zace. 2 Pakuti udzadya za nchito ya manja ako; Wodala iwe, ndipo kudzakukomera. 3 Mkazi wako…

Masalmo 129

Israyeli asautsidwa koma osafafanizidwa Nyimbo yokwerera. 1 Anandisautsa kawiri kawiri kuyambira ubwana wanga, Anene tsono Israyeli; 2 Anandisautsa kawiri kawiri kuyambira ubwana wanga; Koma sanandilaka. 3 Olima analima pamsana panga;…

Masalmo 130

Pemphero lakuti akhululukidwe Nyimbo yokwerera. 1 M’mozamamo ndinakupfuulirani, Yehova. 2 Ambuye, imvani liu langa; Makutu anu akhale cimverere Mau a kupemba kwanga. 3 Mukasunga mphulupulu, Yehova, Adzakhala ciriri ndani, Ambuye?…