Masalmo 111
Alemekeza Mulungu pa nchito zao zazikuru zokoma 1 Haleluya. Ndidzayamika Yehova ndi mtima wonse, Mu upo wa oongoka mtima, ndi mumsonkhano. 2 Nchito za Yehova nzazikuru, Zofunika ndi onse akukondwera…
Alemekeza Mulungu pa nchito zao zazikuru zokoma 1 Haleluya. Ndidzayamika Yehova ndi mtima wonse, Mu upo wa oongoka mtima, ndi mumsonkhano. 2 Nchito za Yehova nzazikuru, Zofunika ndi onse akukondwera…
Adalitsidwa akuopa Mulungu 1 Haleluya. Wodala munthu wakuopa Yehova, Wakukondwera kwambiri ndi malamulo ace, 2 Mbeu yace idzakhala yamphamvu pa dziko lapansi; Mbadwo wa oongoka mtima udzadalitsidwa. 3 M’nyumba mwace…
Anthu onse alemekeze dzina la Mulungu wothandiza aumphawi 1 Haleluya; Lemekezani, inu atumiki a Yehova; Lemekezani dzina la Yehova, 2 Lodala dzina la Yehova. Kuyambira tsopano kufikira kosatha. 3 Citurukire…
Alemekeze Mulungu pa cipulumutso cija ca m’Aigupto 1 M’mene Israyeli anaturuka ku Aigupto, Nyumba ya Yakobo kwa anthu a cinenedwe cacilendo; 2 Yuda anakhala malo ace oyera, Israyeli ufumu wace….
Mulungu ndi wa ulemerero, mafano ndiwo acale 1 Kwa ife ai, Yehova, kwa ife ai, Koma kwa dzina lanu patsani ulemerero, Cifukwa ca cifundo canu, ndi coonadi canu. 2 Aneneranji…
Cikondi ndi ciyamiko ca pa Mulungu cifukwa ca cipalumutso cace 1 Ndimkonda, popeza Yehova amamva, Mau anga ndi kupemba kwanga. 2 Popeza amandicherera khutu lace, Cifukwa cace ndidzaitanira Iye masiku…
Alemekezedwe Mulungu pa cifundo cace 1 Lemekezani Yehova, amitundu onse; Myimbireni, anthu onse. 2 Pakuti cifundo cace ca pa ife ndi cacikuru; Ndi coonadi ca Yehova ncosatha. Haleluya.
Wa Salmo alemekeza Mulungu womlanditsa m’manja mwa adani 1 Yamikani Yehova; pakuti Iye ndiye wabwino; Pakuti cifundo cace ncosatha. 2 Anene tsono Israyeli, Kuti cifundo cace ncosatha. 3 Anene tsono…
Cilamulo ca Mulungu ndi cokometsetsa. Adalitsidwa akucisunga 1 Odala angwiro m’mayendedwe ao, Akuyenda m’cilamulo ca Yehova. 2 Odala iwo akusunga mboni zace, Akumfuna ndi mtima wonse; 3 Inde, sacita cosalungama;…
Apempha Mulungu amlanditse pa Omnamiza Nyimbo yokwerera. 1 Ndinapfuulira kwa Yehova mu msauko wanga, Ndipo anandibvomereza, 2 Yehova, landitsani moyo wanga ku milomo ya mabodza, Ndi ku lilime lonyenga. 3…