Masalmo 101
Davide akuti adzasamala okhulupirika nadzacotsa oipa Salmo la Davide. 1 Ndidzayimba za cifundo ndi ciweruzo; Ndidzayimba zakukulemekezani Inu, Yehova. 2 Ndidzacita mwanzeru m’njira yangwiro; Mudzandidzera liti? Ndidzayenda m’nyumba mwanu ndi…