Masalmo 91
Mulungu asungadi wodzipereka kwa Iye 1 Iye amene akhala pansi m’ngaka yace ya Wam’mwambamwamba Adzagonera mu mthunzi wa Wamphamvuyonse. 2 Ndidzati kwa Yehova, Pothawirapo panga ndi linga langa; Mulungu wanga,…
Mulungu asungadi wodzipereka kwa Iye 1 Iye amene akhala pansi m’ngaka yace ya Wam’mwambamwamba Adzagonera mu mthunzi wa Wamphamvuyonse. 2 Ndidzati kwa Yehova, Pothawirapo panga ndi linga langa; Mulungu wanga,…
Anthu onse ayamike Mulungu cifukwa ca nchito zace, cilungamo cace, ndi cifundo cace Satmo, Nyimbo ya pa Sabata, 1 Nkokoma kuyamika Yehova, Ndi kuyimbira nyimbo dzina lanu, Wam’mwambamwamba Inu: 2…
Ufumu wa Mulungu ndiwo wa ulemerero, mphamvu, ndi ciyero 1 Yehova acita ufumu; wadzibveka ndi ukulu; Wadzibveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m’cuuno; Dziko lomwe lokhalamo anthu likhazikika, silidzagwedezeka. 2 Mpando wacifumu…
Mulungu wolungama adzaweruza otpa 1 Mulungu wakubwezera cilango, Yehova, Mulungu wakubwezera cilango, muoneke wowala. 2 Nyamukani, Inu woweruza wa dziko lapansi: Bwezerani odzikuza coyenera iwo. 3 Oipa adzatumpha ndi cimwemwe…
Adandaulira anthu alemekeze namvere Mulungu wao wamkuru 1 Tiyeni tiyimbire Yehova mokondwera; Tipfuule kwa thanthwe la cipulumutso cathu. 2 Tidze naco ciyamiko pamaso pace, Timpfuulire Iye mokondwera ndi masalmo. 3…
Onse a pansi pano ndi am’mwamba omwe alemekeze Mulungu 1 Myimbireni Yehova nyimbo yatsopano; Myimbireni Yehova, inu, dziko lonse lapansi. 2 Myimbireni Yehova, lemekezani dzina lace; Lalikirani cipulumutso cace tsiku…
Ulemerero wa ufumu wa Mulungu 1 Yehova acita ufumu; dziko lapansi likondwere; Zisumbu zambiri zikondwerere. 2 Pomzinga pali mitambo ndi mdima; Cilungamo ndi ciweruzo ndizo zolimbitsa mpando wacifumu wace. 3…
Alemekeze Mulungu pa cifundo ndi coonadi cao Sa1mo. 1 Myimbireni Yehova nyimbo yatsopano; Popeza anacita zodabwiza: Dzanja lace lamanja, mkono wace woyera, zinamcitira cipulumutso, 2 Yehova anawadziwitsira cipulumutso cace; Anaonetsera…
Mulungu wamkuru wacifundo alemekezedwe 1 Yehova ndiye mfumu; mitundu ya anthu injenjemere; Iye akhala pakati pa akerubi; dziko lapansi ligwedezeke. 2 Yehova ndiye wamkuru m’Ziyoni; Ndipo akwezeka pamwamba pa mitundu…
Olengedwa ndi Mulungu amlemekeze Salmo la Ciyamiko. 1 Pfuulirani kwa Yehova, inu, dziko lonse lapansi. 2 Tumikirani Yehova ndi cikondwerero: Idzani pamaso pace ndi kumyimbira mokondwera, 3 Dziwani kuti Yehova…