Masalmo 1
Kusiyana pakati pa olungama ndi oipa 1 WODALA munthuyo wosayenda mu uphungu wa oipa, Kapena wosaimirira m’njira ya ocimwa, Kapena wosakhala pansi pa bwalo la onyoza. 2 Komatu m’cilamulo ca…
Kusiyana pakati pa olungama ndi oipa 1 WODALA munthuyo wosayenda mu uphungu wa oipa, Kapena wosaimirira m’njira ya ocimwa, Kapena wosakhala pansi pa bwalo la onyoza. 2 Komatu m’cilamulo ca…
Ufumu wa wodzozedwa wa Yehova 1 Aphokoseranji amitundu. Nalingiriranji anthu zopanda pace? 2 Adzikhazikitsa mafumu a dziko lapansi, Nacita upo akulu pamodzi, Kutsutsana naye Yehova, ndi Wodzozedwa wace, ndi kuti….
Kukhulupirika kwa Mulungu Salimo la Davide, muja anathawa Abisalomu mwana wace. 1 Yehova! Ha! acuruka nanga akundisautsa ine! Akundiukira ine ndi ambiri. 2 Ambiri amati kwa moyo wanga, Alibe cipulumutso…
Pemphero posautsidwa Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Nesmoto. Salmo la Davide. 1 Pakupfuula ine mundiyankhe, Mulungu wa cilungamo canga; Pondicepera mwandikulitsira malo: Ndicitireni cifundo, imvani pemphero langa. 2 Amuna inu,…
Matsoka a oipa, madalitso a olungama Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Nekiloto. Salimo la Davide. 1 Mverani mau anga, Yehova, Zindikirani kulingirira kwanga. 2 Tamvetsani mau a kupfuula kwanga, Mfumu…
Davide apempha cifundo kwa Mulungu Kwa Mkulu wa Nyimbo: pa Neginoto, pa Seminiti. Salmo la Davide. 1 Yehova, musandidzudzule mu mkwiyo wanu, Ndipo musandilange m’ukali wanu. 2 Mundicitire cifundo, Yehova;…
Adani amzinga, Davide adziponya kwa Mulungu Syigayoni wa Davide woyimbira Yehova, cifukwa ca mau a Kumi Mbenjamini. 1 Yehova Mulungu wanga, ndakhulupirira Inu: Mundipulumutse kwa onse akundilonda, nimundilanditse; 2 Kuti…
Davide ayimbira ulemerero wa Mulungu, ndi ulemu umene Mulungu acitira mtundu wa anthu Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Oititl. Salnto la Davide. 1 Yehova, Ambuye wathu, Dzina lanu liposadi nanga…
Ayamikira cipulumutso cacikuru Kwa Mkulu wa Nyimbo; pa Mut-laben. Salmo la Davide. 1 Ndidzayamika Yehova ndi mtima wanga wonse; Ndidzawerengera zodabwiza zanu zonse. 2 Ndidzakondwerera ndi kusekera mwa Inu; Ndidzayimbira…
Athamangira Mulungu pothawa adani omtsata 1 Muimiranji patari, Yehova? Mubisaliranji m’nyengo za nsautso? 2 Podzikuza woipa apsereza waumphawi; Agwe m’ciwembu anapanganaco. 3 Pakuti woipa adzitamira cifuniro ca moyo wace, Adalitsa…