Marko 11

Yesu alowa m’Yerusalemu alikukhala pa buru 1 Ndipo pamene iwo anayandikira ku Yerusalemu, ku Betefage ndi Betaniya, pa phiri la Azitona, anatuma awiri a ophunzira ace, 2 nanena nao, Mukani,…

Marko 12

Fanizo La osungira munda 1 Ndipo Iye anayamba kulankhula nao m’mafanizo. Munthu analima munda wamphesa, nauzunguniza ndi linga, nakumba moponderamo mphesa, namanga nsanja, naukongoletsa kwa olima munda, namuka kwina. 2…

Marko 13

Yesu aneneratu za masautso alinkudza 1 Ndipo pamene analikuturuka Iye m’Kacisi, mmodzi wa ophunzira ace ananena kwa Iye, Mphunzitsi, onani, miyala yotere ndi nyumba yotere. 2 Ndipo Yesu anati kwa…

Marko 14

Ansembe akulu acita ciwembu pa Yesu 1 Ndipo popita masiku awiri kuli phwando la Paskha ndi mikate yopanda cotupitsa; ndipo ansembe akuru ndi alembi anafunafuna momcitira ciwembu, ndi kumupha: 2…

Marko 15

Yesu aweruzidwa ndi Pilato 1 Ndipo pomwepo mamawa anakhala upo ansembe akuru, ndi akuru a anthu, ndi alembi, ndi akuru a milandu onse, namanga Yesu, namtenga, nampereka kwa Pilato. 2…

Marko 16

Yesu auka kwa akufa 1 Ndipo litapita Sabata, Maliya wa Magadala, ndi Maliya amace wa Yakobo, ndi Salome, anagula zonunkhira, kuti akadze kumdzoza Iye. 2 Ndipo anadza kumanda mamawa tsiku…