Marko 1

Yohane Mbatizi 1 CIYAMBI cace ca Uthenga Wabwino wa Yesu Kristu, Mwana wa Mulungu. 2 Monga mwalembedwa m’Yesaya mneneri, Ona, ndituma mthenga wanga patsogolo pa nkhope yanu, Amene adzakonza njira…

Marko 2

Aciritsa wodwala manjenje 1 Ndipo polowanso Iye m’Kapernao atapita masiku ena, kunamveka kuti ali m’nyumba. 2 Ndipo ambiri anaunjikana, kotero kuti anasowa malo, ngakhale pakhomo pomwe; ndipo analankhula nao mau….

Marko 3

Yesu aciritsa wa dzanja lopuwala 1 Ndipo analowanso m’sunagoge; ndipo munali munthu m’menemo ali ndi dzanja lace lopuwala. 2 Ndipo anamuyang’anira Iye, ngati adzamciritsa dzuwa la Sabata; kuti ammange mlandu….

Marko 4

Fanizo La wofesa 1 Ndipo anayambanso kuphunzitsa pambali pa nyanja, Ndipo anasonkhana kwa Iye khamu lalikurukuru, kotero kuti analowa Iye mungalawa, nakhala m’nyanja; ndipo khamu lonse linakhala pamtunda m’mbali mwa…

Marko 5

Yesu aciritsa wogwidwa ndi mzimu wonyansa ku Gerasa 1 Ndipo anafika tsidya lina la nyanja, ku dziko la Agerasa, 2 Ndipo pameneadaturuka mungalawa, pomwepo anakomana naye munthu woturuka kumanda wa…

Marko 6

Apeputsa Yesu ku Nazarete 1 Ndipo Iye anaturuka kumeneko; nafika ku dziko la kwao; ndipo ophunzira ace anamtsata. 2 Ndipo pofika dzuwa la Sabata, anayamba kuphunzitsa m’sunagoge; ndipo ambiri anamva…

Marko 7

Miyambo ya makolo ao 1 Ndipo anasonkhana kwa Iye Afarisi, ndi alembi ena, akucokera ku Yerusalemu, 2 ndipo anaona kuti ophunzira ace ena anadya mkate ndi m’manja mwakuda, ndiwo osasamba….

Marko 8

Yesu acurukitsa mikate kaciwiri 1 Masiku ajawo pakukhalanso khamu lalikuru la anthu, ndipo analibe kanthu kakudya, iye anadziitanira ophunzira ace, nanena nao, 2 Ndimva nalo cifundo khamulo, cifukwa ali ndi…

Marko 9

Mawalitsidwe a Yesu paphiri 1 Ndipo ananena nao, Ndithu ndinena ndi inu kuti, Alipo ena akuimirira pano, amene sadzalawa imfa konse, kufikira akaona Ufumu wa Mulungu utadza ndi mphamvu. 2…

Marko 10

Asasiyane mwamuna ndi mkazi wace 1 Ndipo ananyamuka Iye kumeneko, nadza ku maiko a ku Yudeya ndi ku tsidya lija la Yordano; ndipo anasonkhananso kwa Iye makamu a anthu; ndipo…