Maliro 1

Tsoka la Yerusalemu 1 Ha! mudziwo unadzala anthu, ukhalatu pa wokha! Ukunga mkazi wamasiye! Waukuruwo mwa amitundu, kalonga wamkazi m’madera a dziko Wasanduka wolamba! 2 Uliralira usiku; misozi yace iri…

Maliro 2

Yerusalemu amangidwa misasa, njala isautsa, mudzi upasuka 1 Ambuye waphimbatu ndi mtambo mwana wamkazi wa Ziyoni, pomkwiyira! Wagwetsa pansi kucokera kumwamba kukoma kwace kwa Israyeli; Osakumbukira poponda mapazi ace tsiku…

Maliro 3

Yeremiya acita nkhawa, adziponya kwa Yehova 1 Ine ndine munthuyu wakuona msauko ndi ndodo ya ukali wace. 2 Wanditsogolera, nandiyendetsa mumdima, si m’kuunika ai. 3 Zoonadi amandibwezera-bwezera dzanja lace monditsutsa…

Maliro 4

Tsoka a anthu Avuda 1 Ha! golidi wagugadi; golidi woona woposa wasandulika; Miyala ya malo opatulika yakhutulidwa pa malekezero a makwalalaonse. 2 Ana a Ziyoni a mtengo wapatari, olingana ndi…

Maliro 5

Adandaulira Yehova pa tsoka la ukapolo wao 1 Yehova, kumbukirani cotigweraci, Penyani nimuone citonzo cathu. 2 Colowa cathu casanduka ca alendo, Ndi nyumba zathu za acilendo. 3 Ndife amasiye opanda…