Macitidwe 21
Paulo atabwera, ku Yerusalemu amgwira m’Kacisi 1 Ndipo kunali, titalekana nao ndi kukankha ngalawa, tinadza molunjika ku Ko, ndi m’mawa mwace ku Rode, ndipo pocokerapo ku Patara; 2 ndipo m’mene…
Paulo atabwera, ku Yerusalemu amgwira m’Kacisi 1 Ndipo kunali, titalekana nao ndi kukankha ngalawa, tinadza molunjika ku Ko, ndi m’mawa mwace ku Rode, ndipo pocokerapo ku Patara; 2 ndipo m’mene…
Paulo acita codzikanira cace kwa anthu 1 Amuna, abale, ndi atate, mverani codzikanira canga tsopano, ca kwa inu. 2 Ndipo pakumva kuti analankhula nao m’cinenedwe ca Cihebri, anaposa kukhala cete;…
1 Ndipo Paulo, popenyetsetsa a m’bwalo la akuru anati, Amuna, abale, ndakhala ine pamaso pa Mulungu ndi cikumbu mtima cokoma conse kufikira lero lomwe. 2 Ndipo mkulu wa ansembe Hananiya…
Felike amva mlandu wa Paulo 1 Ndipo atapita masiku asanu anatsika mkulu wa ansembe Hananiya pamodzi ndi akuru ena, ndi wogwira moyo dzina lace Tertulo; ndipo anafotokozera kazembeyo za kunenera…
Paulo pa bwalo la miranda la Festo. Anena akaturukira kwa Kaisara 1 Pamenepo Festo m’mene analowa dziko lace, ndipo atapita masiku atatu, anakwera kunka ku Yerusalemu kucokera ku Kaisareya. 2…
1 Ndipo Agripa anati kwa Paulo, Kwaloleka udzinenere wekha. Pamenepo Paulo, anatambasula dzanja nadzikanira: 2 Ndidziyesera wamwai, Mfumu Agripa, popeza nditi ndidzikanira lero pamaso panu, za zonse zimene Ayuda andinenera…
Amtumiza Paulo ku Roma. Tsoka panyanja 1 Ndipo pamene padatsimikizika kuti tipite m’ngalawa kunka ku Italiya, anapereka Paulo ndi andende ena kwa kenturiyo dzina lace Yuliyo, wa gulu la Augusto….
Paulopa Melita 1 Ndipo titapulumuka, pamenepo tinadziwa kuti cisumbuco cinachedwa Melita. 2 Ndipo akunja anaticitira zokoma zosacitika pena ponsepo; pakuti anasonkha moto, natilandira ife tonse, cifukwa ca mvula inalinkugwa, ndi…