Macitidwe 11

Petro adziwerengera pamaso pa Mpingo kuti anabatiza Komeliyo 1 Koma atumwi ndi abale akukhala m’Yudeya anamva kuti amitundunso adalandira mau a Mulungu. 2 Ndipo pamene Petro adakwera kudza ku Yerusalemu,…

Macitidwe 12

Herode azunza Eklesia; amupha Yakobo, naponya Petro kundende. Petro apulumuka m’ndende. Imfa ya Herode 1 Koma nyengo imeneyo Herode mfumu anathira manja ena a m’Eklesia kuwacitira zoipa. 2 Ndipo adapha…

Macitidwe 13

Ulendo woyamba wa Paulo. Mpingo wa ku Antiokeya utuma Paulo ndi Bamaba amuke kwa amitundu, Alalikira pa Kupro, Elima watsenga 1 Ndipo kunali aneneri ndi aphunzioo ku Antiokeya mu Mpingo…

Macitidwe 14

Uthenga Wabwino ulalikidwa ku Ikoniyo, Lustra, ndi Derbe 1 Ndipo kunali pa Ikoniyo kuti analowa pamodzi m’sunagoge wa Ayuda, nalankhula kotero, kuti khamu lalikuru la Ayuda ndi Ahelene anakhulupira. 2…

Macitidwe 15

Ku Yerusalemu atumwi ndi akuru aweruza za mdulidwe ndi malamulo a Mose 1 Ndipo anadza ena akutsika ku Yudeya, nawaphunzitsa abale, nati, Mukapandakudulidwa monga mwambo wa Mose, simungathe kupulumuka. 2…

Macitidwe 16

1 Ndipo anafikanso ku Derbe ndi Lustra; ndipo taonani, panali wophunzira wina pamenepo, dzina lace Timoteo, amace ndiye Myuda wokhulupira; koma atate wace ndiye Mhelene. 2 Ameneyo anamcitira umboni wabwino…

Macitidwe 17

Paulo ku Tesalonika ndi Bereya 1 Pamene anapitirira pa Amfipoli, ndi Apoloniya, anafika ku Tesalonika, kumene kunali sunagoge wa Ayuda. 2 Ndipo Paulo, monga amacita, analowa kwa iwo; ndipo masabata…

Macitidwe 18

Paulo ku Korinto ndi ku Efeso, Abwera ku Yerusalemu 1 Zitapita izi anacoka ku Atene, nadza ku Korinto. 2 Ndipo anapeza Myuda wina dzina lace Akula, pfuko lace la ku…

Macitidwe 19

Ulendo wacitatu wa Paulo. Demetrio autsa phokoso 1 Ndipo panali, pamene Apolo anali ku Korinto, Paulo anapita pa maiko a pamtunda, nafika ku Efeso, napeza akuphunzira ena; 2 ndipo anati…

Macitidwe 20

Paulo apitanso ku Makedoniya; ndi Helene, ndi Asiya 1 Ndipo litaleka phokoso, Paulo anaitana ophunzirawo, ndipo m’mene anawacenjeza, analawirana nao, naturuka kunka ku Makedoniya. 2 Ndipo m’mene atapitapita m’mbali zijazo,…