Macitidwe 1
Yesu akwera kunka Kumwamba 1 TAONANI Teofilo inu, mau aja oyamba ndinakonza, za zonse Yesu anayamba kuzicita ndi kuziphunzitsa, 2 kufikira tsiku lija anatengedwa kunka Kumwamba, atatha kulamulira mwa Mzimu…
Yesu akwera kunka Kumwamba 1 TAONANI Teofilo inu, mau aja oyamba ndinakonza, za zonse Yesu anayamba kuzicita ndi kuziphunzitsa, 2 kufikira tsiku lija anatengedwa kunka Kumwamba, atatha kulamulira mwa Mzimu…
Tsiku la Pentekoste 1 Ndipo pakufika tsiku la Penteskoste, anali onse pamodzi pa malo amodzi. 2 Ndipo mwadzidzidzi anamveka mau ocokera Kumwamba ngati mkokomo wa mphepo yolimba, nadzaza nyumba yonse…
Wopunduka cibadwire aciritsidwa. Conenera Petro m’Kacisi 1 Koma Petro ndi Yohane analikukwera kunka kuKacisi pa ora lakupembedza, ndilo lacisanu ndi cinai. 2 Ndipo munthu wina wopunduka miyendo cibadwire ananyamulidwa, amene…
Petro ndi Yohane ku bwalo la akuru 1 Koma m’mene analikulankhula ndi anthu, ansembe ndi mdindo wa kuKacisi ndi Asaduki anadzako, 2 obvutika mtima cifukwa anaphunzitsa anthuwo, nalalikira mwa Yesu…
Za Hananiya ndi Safira 1 Koma munthu wina dzina lace Hananiya pamodzi ndi Safira mkazi wace, 2 anagulitsa cao, napatula pa mtengo wace, mkazi yemwe anadziwa, natenga cotsala, naciika pa…
Asankha atumiki asanu ndi awiri 1 Koma masiku awo, pakucurukitsa ophunzira, kunauka cidandaulo, Aheleniste kudandaula pa Ahebri, popeza amasiye ao anaiwalika pa citumikiro ca tsiku ndi tsiku. 2 Ndipo khumi…
1 Ndipo mkulu wa ansembe anati, Zitero izi kodi? 2 Ndipo Stefano anati, Amuna inu, abale, ndi atate, tamverani. Mulungu wa ulemerero anaonekera kwa kholo lathu Abrahamu, pokhala iye m’Mesopotamiya,…
Uthenga Wabwino pa Samariya. Simoni wanyanga 1 Ndipo Saulo analikubvomerezana nao pa imfa yace. Ndipo tsikulo kunayamba kuzunza kwakukuru pa Mpingo unali m’Yerusalemu; ndipo anabalalitsidwa onse m’maiko a Yudeya ndi…
Kusandulika mtima kwa Paulo pa njira ya ku Damasiko 1 Koma Saulo, wosaleka kupumira pa akuphunzira a Ambuye kuopsya ndi kupha, ananka kwa mkulu wa ansembe, 2 napempha kwa iye…
Kenturiyo Komeliyo 1 Ndipo kunali munthu ku Kaisareya, dzina lace Komeliyo, kenturiyo wa gulu lochedwa la Italiya, 2 ndiye munthu wopembedza, ndi wakuopa Mulungu ndi banja lace lonse, amene anapatsa…