Luka 21
Mphatso ya mkazi wamasiye 1 Ndipo Yesu anakweza maso, naona anthu eni cuma alikuika zopereka zao mosungiramo ndalama. 2 Ndipo anaona mkazi wina wamasiye waumphawi alikuika momwemo timakobiri tiwiri. 3…

Yudase apangana kupereka Yesu 1 Ndipo phwando la mikate yopanda cotupitsa linayandikira, ndilo lochedwa Paskha. 2 Ndipo ansembe akuru ndi alembi anafunafuna maphedwe ace pakuti anaopa anthuwoo. 3 Ndipo Satana…
Yesu na bwalo la Pilato 1 Ndipo khamu lonselo Iinanyamuka kupita naye kwa Pilato. 2 Ndipo anayamba kumnenera iye, kuti, Tinapeza munthu uyu alikupandutsa anthu a mtundu wathu, ndi kuwaletsa…
Yesu auka kwa akufa 1 Koma tsiku loyamba la sabata, mbanda kuca, anadza kumanda atatenga zonunkhira adazikonza. 2 Ndipo anapeza mwala unakunkhunizidwa kuucotsa pamanda. 3 Ndipo m’mene analowa sanapeza mtembo…