Luka 1
1 POPEZA ambiri anayesa kulongosola nkhani ya zinthu zinacitika pakati pa ife, 2 monga anazipereka kwa ife iwo amene anakhala mboni ndi atumiki a mau, 3 kuyambira paciyambi, ndinayesa nkokoma…
1 POPEZA ambiri anayesa kulongosola nkhani ya zinthu zinacitika pakati pa ife, 2 monga anazipereka kwa ife iwo amene anakhala mboni ndi atumiki a mau, 3 kuyambira paciyambi, ndinayesa nkokoma…
Kubadwa kwa Yesu Kristu 1 Ndipo kunali masiku aja, kuti lamulo linaturuka kwa Kaisara Augusto kuti dziko lonse lokhalamo anthu lilembedwe; 2 ndiko kulembera koyamba pokhala Kureniyo kazembe wa Suriya….
Kulalikira kwa Yohane Mbatizi 1 Ndipo pa caka cakhumi ndi cisanu ca ufumu wa Tiberiyo Kaisara, pokhala Pontiyo Pilato kazembe wa Yudeya, ndi Herode ciwanga ca Galileya, ndi Filipo mbale…
Kuyesedwa kwa Yesu 1 Ndipo Yesu, wodzala ndi Mzimu Woyera, anabwera kucokera ku Yordano, natsogozedwa ndi Mzimu kunka kucipululu kukayesedwa ndi mdierekezi masiku makumi anai. 2 Ndipo iye sanadya kanthu…
Asodzi athandizidwa ndi Yesu, namtsata 1 Ndipo panali, pakumkanikiza khamu la anthu, kudzamva mau a Mulungu, iye analikuimirira m’mbali mwa nyanja ya Genesarete; 2 ndipo anaona ngalawa ziwiri zinakhala m’mbali…
Yesu Mbuye wa tsiku la Sabata 1 Ndipo kunali tsiku la Sabata, iye analinkupita pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ace analinkubudula ngala za tirigu, nazifikisa m’manja mwao, nadya….
Kenturiyo wa ku Kapernao 1 Pamene Yesu adamariza mau ace onse m’makutu a anthu, analowa m’Kapernao. 2 Ndipo kapolo wa kenturiyo, wokondedwa naye, anadwala, nafuna kutsirizika. 3 Ndipo pamene iye…
Akazi otumikira Yesu ndi cuma cao 1 Ndipo kunali, katapita kamphindi anayendayenda kumizinda ndi kumidzi, kulalikira ndi kuwauza U thenga Wabwino wa Ufumu wa Mulungu, ndi pamodzi naye khumi ndi…
Yesu atuma ophunzira ace kukalalikira mau 1 Ndipo iye anaitana pamodzi khumi ndi awiriwo nawapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse, ndi zakuciritsa nthenda. 2 Ndipo anawatuma kukalalikira Ufumu wa…
Yesu atuma ophunzira makumi asanu ndi awiri 1 Zitatha izi Ambuye anaika ena makumi asanu ndi awiri, nawatuma iwo awiri awiri pamaso pace ku mudzi uli wonse, ndi malo ali…