Levitiko 21
Za kupatulika kwa ansembe 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, Nena ndi ansembe, ana a Aroniwo, nuti nao, Asadzidetse mmodzi wa inu cifukwa ca wakufa mwa anthu a mtundu wace;…
Za kupatulika kwa ansembe 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, Nena ndi ansembe, ana a Aroniwo, nuti nao, Asadzidetse mmodzi wa inu cifukwa ca wakufa mwa anthu a mtundu wace;…
Ansembe ayere pakudya zopatulika 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Nena ndi Aroni ndi ana ace amuna, kuti azikhala padera ndi zinthu zopatulika za ana a Israyeli,…
Za nyengo zoikika za Yehova 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Nyengo zoikika za Yehova zimene muzilalikira zikhale masonkhano opatulika,…
Za mafuta a nyalizo ndi mkate woonekera 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Uza ana a Israyeli, kuti akutengere mafuta a azitona oyera opera akuunikira, kuti aziwalitsa…
Za caka copumula dziko 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose m’phiri la Sinai, ndi kuti, 2 Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Mutakalowa m’dziko limene ndikupatsani, dzikoli lizisungira Yehova…
Malamulo, malonjezo, ndi macenjezo 1 Musamadzipangira mafano, kapena kudziutsira mafano osema, kapena coimiritsa, kapena kuika mwala wozokota m’dziko mwanu kuugwadira umene; popeza Ine ndine Yehova Mulungu wanu. 2 Musunge masabata…
Cowinda ndi ciombolo cace 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Pamene munthu acita cowinda ca padera, anthuwo azikhala a Yehova…