Levitiko 11
Za nyama zodyeka ndi zosadyeka ndi zakufa zodetsa munthu 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati nao, 2 Nenani ndi ana a Israyeli, ndi kuti, Izi ndi zamoyo…
Za nyama zodyeka ndi zosadyeka ndi zakufa zodetsa munthu 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati nao, 2 Nenani ndi ana a Israyeli, ndi kuti, Izi ndi zamoyo…
Za kuyeretsedwa kwa mkazi 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Nena ndi ana a Israyeli, ndi kuti, Akaima mkazi, nakabala mwana wamwamuna, adzakhala wodetsedwa masiku asanu ndi awiri;…
Malamulo a pa nthenda yakhate 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati, 2 Ngati munthu ali naco cotupa, kapena nkhanambo, kapena cikanga pa khungu la thupi lace, ndipo…
Malamulo a pa kumyeretsa wakhate 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose nati, 2 Cilamulo ca wakhate tsiku la kumyeretsa kwace ndi ici: azidza naye kwa wansembe; 3 ndipo wansembe aturuke…
Ndipo Yehova ananena ndi 1 Mose ndi Aroni, nati, 2 Nenani nao ana a Israyeli, nimuti nao, Pamene mwamuna ali yense ali ndi nthenda yakukha m’thupi mwace, akhale wodetsedwa, cifukwaca…
Za tsiku lotetezera caka ndi caka 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, atamwalira ana amuna awiri a Aroni, muja anasendera pamaso pa Yehova, namwalira; 2 ndipo Yehova anati kwa Mose,…
Popereka nsembe 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Nena ndi Aroni, ndi ana ace amuna, ndi ana a Israyeli onse, nuti nao, Ici ndi cimene Yehova wauza, ndi…
Malamulo a pa ulemu 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Ine ndine Yehova Molungu wanu. 3 Musamacita monga mwa macitidwe a…
Malamulo ena osiyanasiyana 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Nena ndi khamu lonse la ana a Israyeli, nuti nao, Muzikhala oyera; pakuti ine ndine Yehova Mulungu wanu,…
Ziletsedwa cipembedzo ca Moleke ndi zoipa zina 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Unenenso kwa ana a Israyeli ndi kuti, Ali yense wa ana a Israyeli, kapena…