Hoseya 11

Kusayamika kwa Israyeli; macenjezo ndi malonjezo 1 Pamene Israyeli anali mwana, ndinamkonda, ndinaitana mwana wanga ali m’Aigupto. 2 Monga anawaitana, momwemo anawacokera; anaphera nsembe Abaala, nafukizira mafano osema. 3 Koma…

Hoseya 12

Mlandu wa Yehova pa Israyeli ndi Yuda 1 Efraimu akudya mphepo, natsata mphepo ya kum’mawa; tsiku lonse acurukitsa mabodza ndi cipasuko, ndipo acita pangano ndi Asuri, natenga mafuta kumka nao…

Hoseya 13

Cimo la Israyeli ndi kulangidwa kwace 1 Pamene Bfraimu analankhula panali kunjenjemera; anadzikweza m’Israyeli; koma pamene anaparamula mwa Baala, anafa. 2 Ndipo tsopano aonjeza kucimwa, nadzipangira mafano oyenga a siliva…

Hoseya 14

Mulungu adandaulira Israyeli alape, nalonjeza kuwakhululukira 1 Israyeli, bwerera kumka kwa Yehova Mulungu wako; pakuti wagwa mwa mphulupulu yako. 2 Mukani nao mau, nimubwerere kwa Yehova; nenani kwa Iye, Cotsani…