Hoseya 1

Hoseya akwatira mkazi woipa kufanizira zoipa za Israyeli 1 MAU a Yehova amene anadza kwa Hoseya mwana wa Beeri masiku a Uziya, Yotamu, Ahazi, ndi Hezekiya, mafumu a Yuda, ndi…

Hoseya 2

1 Nenani kwa abale anu, Anthu anga, ndi kwa alongo anu, Wocitidwa-cifundo. 2 Mutsutsane naye mai wanu, mutsutsane naye; pakuti sali mkazi wanga, ndi Ine sindiri mwamuna wace; ndipo acotse…

Hoseya 3

Akwatiranso mkazi woipa, kufaniziranso zocita ana a Israyeli 1 Ndipo Yehova anati kwa ine, Mukanso, konda mkazi wokondedwa ndi bwenzi lace, koma wakucita cigololo monga Yehova akonda ana a Israyeli,…

Hoseya 4

Mlandu pakati pa Mulungu ndi Israyeli 1 Imvani mau a Yehova, inu ana a Israyeli; pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi okhala m’dziko, popeza palibe coonadi, kapena cifundo, kapena kudziwa…

Hoseya 5

Kulowerera kwa Israyeli 1 Imvani ici, ansembe inu; mverani, inu nyumba ya Israyeli; cherani khutu, inu nyumba ya mfumu; pakuti ciweruzoci cinena inu; pakuti munakhala msampha ku Mizipa, ndi ukonde…

Hoseya 6

Israyeli abwerera kunka kwa Yehova 1 Tiyeni, tibwerere kunka kwa Yehova; pakuti wang’amba, nadzatipoletsera; wakantha, nadzatimanga. 2 Atapita masiku awiri adzatitsitsimutsa, tsiku lacitatu adzatiutsa; ndipo tidzakhala ndi moyo pamaso pace….

Hoseya 7

Kucimwa ndi kupandukira kwa Israyeli 1 M’mene ndiciritsa Israyeli, mphulupulu ya Efraimu ibvumbuluka, ndi zoipa za Samariya; pakuti acita bodza, ndipo mkhungu alowa m’nyumba, ndi gulu la mbala manca kubwalo….

Hoseya 8

Kupembedza mafano ndi kusamvera kwa Israyeli 1 Lipenga kukamwa kwako, Akudza ngati ciombankhanga, kulim bana ndi nyumba ya Yehova; cifukwa analakwira cipangano canga, napikisana naco cilamulo canga. 2 Adzapfuulira kwa…

Hoseya 9

Cimo la Israyeli ndi zotsatira zace 1 Usakondwera, Israyeli, ndi kusekerera, ngati mitundu ya anthu; pakuti wacita cigololo kuleka Mulungu wako, wakonda mphotho ya cigololo pa dwale la tirigu liri…

Hoseya 10

1 Israyeli ndi mpesa wotambalala, wodzibalira wokha zipatso; monga umo zinacurukira zipatso zace, momwemo anacurukitsa maguwa a nsembe ace; monga mwa kukoma kwace kwa dziko lace anapanga zoimiritsa zokoma. 2…