Ezekieli 11
Ciweruzo ca Mulungu pa mafumu a Ayuda 1 Pamenepo unandikweza mzimu, nudza nane ku cipata ca kum’mawa ca nyumba ya Yehova coloza kum’mawa; ndipo taonani, pa citseko ca cipata amuna…
Ciweruzo ca Mulungu pa mafumu a Ayuda 1 Pamenepo unandikweza mzimu, nudza nane ku cipata ca kum’mawa ca nyumba ya Yehova coloza kum’mawa; ndipo taonani, pa citseko ca cipata amuna…
Khoma labooledwa lofanizira ukapolo ndi ubalaliko wao 1 Mau a Yehova anandidzeranso, ndi kuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, ukhala pakati pa nyumba yampanduko, yokhala nao maso akuonera, koma osaona;…
1 Ndipo mau a Yehova anandidzera ine, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, Unenere za aneneri a Israyeli onenerawo, nuziti nao onenera za m’mtima mwao mwao, Tamverani mau a Yehova….
Cilango ca pa opembedza mafano 1 Pamenepo anafika kwa ine akulu ena a Israyeli nakhala pansi pamaso panga. 2 Ndipo anandidzera mau a Yehova, akuti, 3 Wobadwa ndi munthu iwe,…
Mtengo wopanda pace 1 Ndipo anandidzera mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, mtengo wampesa uposeranji mtengo uli wonse wina, nthambi ya mpesa yokhalayo mwa mitengo ya kunkhalango?…
Kusakhulupirika kwa Yerusalemu 1 Anandidzeranso mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, Dziwitsa Yerusalemu zonyansa zace, nuziti, 3 Atero Ambuye Yehova kwa Yerusalemu, Ciyambi cako ndi kubadwa kwako…
Fanizo la ziombankhanga ziwiri ndi mpesa 1 Ndipo anandidzera mau a Yehova, akuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, ipha mwambi, nunene fanizo kwa nyumba ya Israyeli, 3 nuziti, Atero Ambuye…
Udindo ndi wace wace wa munthu 1 Ndipo anandidzera mau a Yehoya, akuti, 2 Mutani inu ndi kunena mwambi uwu za dziko la Israyeli, wakuti, Atate adadya mphesa zosacha, ndi…
Fanizo la mkango waukazi, ndi la mpesa 1 Ndipo iwe, takwezera akalonga a Israyeli nyimbo ya maliro, 2 uziti, Mai wako ndi ciani? Mkango waukazi unabwanthama mwa mikango, unalera ana…
Macimo a Aisrayeli citurukire iwo m’dziko la Aigupto 1 Ndipo kunali caka cacisanu ndi ciwiri, mwezi wacisanu; tsiku lakhumi la mwezi, anadza akulu ena a Israyeli kufunsira kwa Yehova, nakhala…