Ezekieli 1

Masomphenya a Ezekieli 1 NDIPO kunali caka ca makumi atatu, mwezi wacinai, tsiku lacisanu la mwezi, pokhala ine pakati pa andende kumtsinje Kebara, kunatseguka kumwamba, ndipo ndinaona masomphenya a Mulungu….

Ezekieli 2

Kuitanidwa kwa Ezekieli 1 Ndipo anati kwa ine, Wobadwa ndi munthu iwe, khala ciriri, ndipo ndidzanena nawe. 2 Ndipo unandilowa mzimu pamene ananena nane, ndi kundiimika ndikhale ciriri; ndipo ndinamumva…

Ezekieli 3

1 Ndipo ananena nane, Wobadwa ndi munthu iwe, Idya cimene wacipeza; idya mpukutu uwu, numuke ndi kunena ndi nyumba ya Israyeli. 2 Pamenepo ndinatsegula pakamwa panga ndipo anandidyetsa mpukutuwo. 3…

Ezekieli 4

Aneneratu mophiphiritsa za kumangidwa misasa Yerusalemu 1 Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, dzitengere njerwa, nulike pamaso pako, nulembepo mudzi, ndiwo Yerusalemu; 2 nuuzinge, nuumangire nsanja zouzinga, nuundire nthumbira, ndi kuumangira…

Ezekieli 5

1 Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, udzitengere mpeni wakuthwa, ndiwo lumo la wometa, udzitengere ndi kulipititsa pamutu pako ndi pa ndebvu zako; nudzitengere muyeso kuyesa nao, ndi kugawa tsitsilo. 2…

Ezekieli 6

Aneneratu motsutsa mapiri a Israyeli 1 Ndipo mau a Yehova anandidzera, kuti, 2 Wobadwa ndi munthu iwe, lozetsa nkhope yako ku mapiri a Israyeli, uwanenere, 3 nunene, Mapiri a Israyeli…

Ezekieli 7

Kutha kwace kwa dziko la Israyeli 1 Ndipo mau a Yehova anandidzera, akuti, 2 Ndipo iwe wobadwa ndi munthu, atero Ambuye Yehova kwa dziko la Israyeli, Kwatha; kwafika kutha kwace…

Ezekieli 8

Masomphenya a zoipitsitsa za m’Kacisi 1 Ndipo kunali caka cacisanu ndi cimodzi, mwezi wacisanu ndi cimodzi, tsiku lacisanu la mweziwo, pokhala ine m’nyumba mwanga, akulu a Yuda omwe analikukhala pamaso…

Ezekieli 9

Malango apa ocimwa 1 Pamenepo Iye anapfuula m’makutu mwanga ndi mau akuru, ndi kuti, Asendere oyang’anira mudzi, ali yense ndi cida cace coonongera m’dzanja lace. 2 Ndipo taonani, anadza amuna…

Ezekieli 10

Masomphenya a akerubi 1 Ndipo ndinapenya, ndipo taonani, ku thambo lokhala pamwamba pa mitu ya akerubi kudaoneka ngati mwala wasafiro, ngati maonekedwe a cifaniziro ca mpando wacifumu pamwamba pao. 2…