Ezara 1
Mulungu apangira Koresi alole Ayuda abwere kwao kukamanga Kacisi 1 CAKA coyamba tsono ca Koresi mfumu ya ku Perisiya, kuti akwaniridwe mau a Yehova m’kamwa mwa Yeremiya, Yehova anautsa mzimu…
Mulungu apangira Koresi alole Ayuda abwere kwao kukamanga Kacisi 1 CAKA coyamba tsono ca Koresi mfumu ya ku Perisiya, kuti akwaniridwe mau a Yehova m’kamwa mwa Yeremiya, Yehova anautsa mzimu…
Maina a Ayuda obwera ku Yerusalemu ndi Zerubabele 1 Ana a deralo, amene anakwera kuturuka m’ndende mwa andende aja Nebukadinezara mfumu ya Babulo adawatenga ndende kumka nao ku Babulo, nabwerera…
Limangidwa guwa la nsembe 1 Utakhala tsono mwezi wacisanu ndi ciwiri, ana a Israyeli ali m’midzimo, anthuwo anasonkhana ngati munthu mmodzi ku Yerusalemu. 2 Nanyamuka Yesuwa mwana wa Yozadaki, ndi…
Asamariya aneneza Ayuda omanga Kacisi kwa Ahaswero 1 Atamva tsono a adani Yuda ndi Benjamini kuti ana aja a ndende analikumangira Yehova Mulungu wa Israyeli Kacisi, 2 anayandikira kwa Zerubabele,…
Zerubabele ndi Yesuwa apitirira kumanga Kacisi 1 Ndipo aneneri, Hagai mneneriyo, ndi Zekariya mwana wa Ido, ananenera kwa Ayuda okhala m’Yuda ndi m’Yerusalemu; m’dzina la Mulungu wa Israyeli ananenera kwa…
Dariyo anenetsa kuti Kacisi amangidwe 1 Pamenepo analamulira Dariyo mfumu, ndipo anthu anafunafuna m’nyumba ya mabuku mosungira cuma m’Babulo. 2 Napeza ku Akimeta m’nyumba ya mfumu m’dera la Mediya, mpukutu,…
Aritasasta atumiza Ezara ku Yerusalemu akonzenso cipembedzo ca Yehova 1 Zitatha izi tsono, pokhala mfumu Aritasasta mfumu ya Perisiya, anadza Ezara mwana wa Seraya, mwana wa Azariya, mwana wa Hilikiya,…
Maina a opita ndi Ezara. Ulendo wao mpaka Yerusalemu 1 Ndipo akuru a nyumba za makolo ndi awa, ndi cibadwidwe ca iwo okwera nane limodzi kucokera ku Babulo, pokhala mfumu…
Mwankhawa Ezara apempherera Ayuda okwatira acilendo kwa Mulunzu 1 Zitatha izi tsono anandiyandikira akalonga, ndi kuti, Anthu a Israyeli, ndi ansembe, ndi Alevi, sanadzilekanitsa ndi anthu a maikowa, kunena za…
Acotsedwa akazi acilendo 1 Pakupemphera Ezara tsono, ndi kuulula ndi kulira misozi, ndi kudzigwetsa pansi pakhomo pa nyumba ya Mulungu, udamsonkhanira mwa Israyeli msonkhano waukuru ndithu wa amuna, ndi akazi,…