Estere 1
Madyerero a Ahaswero 1 IZI zinacitika masiku a Ahaswero, ndiye Ahasweroyo anacita ufumu kuyambira Indiya kufikira Kusi, pa maiko zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi awiri. 2 Masiku…
Madyerero a Ahaswero 1 IZI zinacitika masiku a Ahaswero, ndiye Ahasweroyo anacita ufumu kuyambira Indiya kufikira Kusi, pa maiko zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi awiri. 2 Masiku…
Ahaswero akwatira Estere 1 Zitatha izi, utaleka mkwiyo wa mfumu Ahaswero, anakumbukila Vasiti, ndi cocita iye, ndi comlamulidwira. 2 Pamenepo anyamata a mfumu omtumikira anati, Amfunire mfumu anamwali okongola; 3…
Moredekai akana kugwadira Hamani 1 Zitatha izi, mfumu Ahaswero anamkuza Hamani mwana wa Hamedata, wa ku Agagi, namkweza, naika mpando wace upose akalonga onse okhala naye. 2 Ndipo anyamata onse…
Moredekai adandaulira Estere anenere Ayuda kwa mfumu 1 Koma podziwa Moredekai zonse zidacitikazi, Moredekai anang’amba zobvala zace, nabvala ciguduli ndi mapulusa, naturuka pakati pa mudzi, napfuula, nalira kulira kwakukuru ndi…
Estere alowa kwa mfumu nampempha iye ndi Hamani azidya naye 1 Ndipo kunali tsiku lacitatu, Estere anabvala zobvala zace zacifumu, nakaimirira m’bwalo la m’kati la nyumba ya mfumu, popenyana pa…
Ahaswero aona cifukwa ca kucitira Moredekai ulemu 1 Usiku uja tulo tidamwazikira mfumu, niti abwere nalo buku la mbiri, naliwerenga pamaso pa mfumu. 2 Napeza mudalembedwa kuti Moredekai adaulula za…
Hamani aululidwa napacikidwa 1 Motero inadza mfumu ndi Hamani kumwa naye mkazi wamkuru Estere. 2 Nitinso mfumu kwa Estere tsiku laciwirili pa madyerero a vinyo, Pempho lanu nciani, mkazi wamkuru…
Ahaswero abvomereza pempho la Estere, Ayuda napulumuka 1 Tsiku lomwelo mfumu Ahaswero anampatsa mkazi wamkuru Estere nyumba ya Hamani mdani wa Ayuda, Nafika Moredekai pamaso pa mfumu; pakuti Estere adamuuza…
Ayuda awapha adani ao 1 Mwezi wakhumi ndi ciwiri tsono, ndiwo mwezi wa Adara, tsiku lace lakhumi ndi citatu, mau a mfumu ndi lamulo lace ali pafupi kucitika, tsikuli adani…
Ukuru wa Moredekai 1 Ndipo mfumu Ahaswero inasonkhetsa dziko, ndi zisumbu za ku nyanja yamcere. 2 Ndi zocita zonse za mphamvu yace, ndi nyonga zace, ndi mafotokozedwe a ukulu wa…