Deuteronomo 31
Yoswa adzalowa m’malo a Mose 1 Ndipo Mose anamuka nanena mau awa kwa Israyeli wonse, 2 nati nao, Ndine munthu wa zaka zana ndi makumi awiri lero lino; sindikhozanso kuturuka…
Yoswa adzalowa m’malo a Mose 1 Ndipo Mose anamuka nanena mau awa kwa Israyeli wonse, 2 nati nao, Ndine munthu wa zaka zana ndi makumi awiri lero lino; sindikhozanso kuturuka…
Nyimbo adailemba Mose 1 Kumwamba kuchere khutu, ndipo ndidzanena; Ndi dziko lapansi limve mau a m’kamwa mwanga; 2 Ciphunzitso canga cikhale ngati mvula; Maneno anga agwe ngati mame; Ngati mvula…
Mose adalitsa mafuko 12 a Israyeli asanafe 1 Ndipo mdalitso, Mose munthu wa Mulungu anadalitsa nao ana a Israyeli asanafe, ndi uwu. 2 Ndipo anati, Yehova anafuma ku Sinai, Nawaturukiraku…
1 Ndipo Mose anakwera kucokera ku zidikha za Moabu, kumka ku phiri la Nebo, pamwamba pa Pisiga, popenyana ndi Yeriko. Ndipo Yehova anamuonetsa dziko lonse la Gileadi, kufikira ku Dani;…