Deuteronomo 11

1 Cifukwa cace muzikonda Yehova Mulungu wanu, ndi kusunga cilangizo cace, ndi malemba ace, ndi maweruzo ace, ndi malamulo ace, masiku onse. 2 Ndipo dziwani lero lino; pakuti sindinena ndi…

Deuteronomo 12

Malo Oyera akhale amodzi 1 Awa ndi malemba ndi maweruzo, muziwasamalirawa kuwacita m’dziko limene Yehova Mulungu wa makolo anu anakupatsani likhale lanu lanu, masiku onse akukhala ndi moyo inu pa…

Deuteronomo 13

Acenjere nao owanyenga kuwapembedzetsa mafano 1 Akauka pakati pa inu mneneri, kapena wakulota maloto, nakakupatsani cizindikilo kapena cozizwa; 2 ndipo cizindikilo kapena cozizwa adanenaci cifika, ndi kuti, Titsate milungu yina,…

Deuteronomo 14

Za nyama yodyedwa ndi yosadyedwa 1 Inu ndinu ana a Yehova Mulungu wanu; musamadziceka, kapena kumeta tsitsi pakati pa maso cifukwa ca akufa. 2 Popeza ndinu mtundu wa anthu opatulikira…

Deuteronomo 15

Za caka ca cilekerero 1 Pakutha Pace pa zaka zisanu ndi ziwiri pakhale cilekerero. 2 Cilekereroco ndici: okongoletsa onse alekerere cokongoletsa mnansi wace; asacifunse kwa mnansi wace, kapena mbale wace;…

Deuteronomo 16

Madyerero a Paskha, a Masabata, ndi a Misasa 1 Samalirani mwezi wa Abibu, kuti muzicitira Yehova Mulungu wanu Paskha; popeza m’mwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakuturutsani m’dziko la Aigupto…

Deuteronomo 17

1 Musamaphera Yehova Mulungu wanu nsembe ya ng’ombe, kapena nkhosa, yokhala naco cirema, kapena ciri conse coipa; pakuti cinyansira Yehova Mulungu wanu. 2 Akapeza pakati panu, m’mudzi wanu wina umene…

Deuteronomo 18

Zoyenera ansembe ndi Alevi 1 Ansembe Alevi, pfuko lonse la Levi, alibe gawo kapena colowa pamodzi ndi Israyeli; azizidya nsembe zamoto za Yehova, ndi colowa cace, 2 Alibe colowa pakati…

Deuteronomo 19

Za midzi yopulumukirako 1 Pamene Yehova Mulungu wanu ataononga amitundu, amene Yehova Mulungu wanu akupatsani dziko lao, ndipo mutalilandira lanu lanu, ndi kukhala m’midzi mwao, ndi m’nyumba zao; 2 pamenepo…

Deuteronomo 20

Malamulo a kunkhondo 1 Pamene muturuka pa mdani wanu kunkhondo, ndi kuona akavalo ndi magareta ndi anthu akucurukira inu, musawaopa; popeza Yehova Mulungu wanu, amene anakukwezani kukuturutsani m’dziko la Aigupto,…