Deuteronomo 1
Mose awafotokozera za ulendo wao m’cipululu 1 AWA ndi mau amene Mose ananena kwa Israyeli wonse, tsidya la Yordano m’cipululu, m’cidikha ca pandunji pa Sufu, pakati pa Parani, ndi Tofeli,…
Mose awafotokozera za ulendo wao m’cipululu 1 AWA ndi mau amene Mose ananena kwa Israyeli wonse, tsidya la Yordano m’cipululu, m’cidikha ca pandunji pa Sufu, pakati pa Parani, ndi Tofeli,…
1 Pamenepo tinabwerera, ndi kuyenda kumka kucipululu, kutsata njira ya Nyanja Yofiira, monga Yehova adanena ndi ine; ndipo tinapaza phiri la Seiri masiku ambiri. 2 Ndipo Yehova ananena ndi ine,…
1 Pamenepo tinatembenuka, ndi kubwera kumka njira ya ku Basana; ndipo Ogi mfumu ya Basana anaturuka kukomana nafe, kugwirana nafe nkhondo, iye ndi anthu ace onse, ku Edrei. 2 Ndipo…
Mose awadandaulira amvere Malamulo a Mulungu 1 Ndipo tsopano, Israyeli, dioloketu tamverani malemba ndi maweruzo, amene ndikuphunzitsani muwacite; kuti mukhale ndi moyo, ndi kulowa, ndi kulandira dziko limene Yehova Mulungu…
Mose abwereza kuwachulira Malamulo a Mulungu 1 Ndipo Mose anaitana Israyeli wonse, nanena nao, Tamverani, Israyeli, malemba ndi maweruzo ndinenawa m’makutu mwanu lero, kuti muwaphunzire, ndi kusamalira kuwacita. 2 Yehova…
Awapempha asunge Malamulo a Mulungu kuti adale 1 Ndipo awa ndi malamulo, malemba, ndi maweruzo, amene Yehova Mulungu wanu analamulira kukuphunzitsani, kuti muziwacita m’dziko limene muolokerako kulilandira; 2 kuti muope…
Awapangira za Akanani ndi zipembedzo zao 1 Pamene Yehova Mulungu wanu atakulowetsani m’dziko limene mumkako kulilandira likhale lanu lanu, ndipo atakataya amitundu ambiri pamaso panu, Ahiti, ndi Agirigazi, ndi Aamori,…
Akumbuke zokoma zazikuru Mulungu anawacitira 1 Muzisamalira kucita malamulo onse amene ndikuuzani lero lino, kuti mukhale ndi moyo, ndi kucuruka, ndi kulowa, ndi kulandira dziko limene Yehova analumbirira makolo anu….
1 Imvani Israyeli; mulikuoloka Yordano lero lino, kulowa ndi kulandira amitundu akuru ndi amphamvu akuposa inu, midzi yaikuru ndi ya malinga ofikira kuthambo, 2 anthu akuru ndi atalitali, ana a…
Za magome aciwiri a Malamulo 1 Masiku aja Yehova anati kwa ine, Dzisemere magome awiri amiyala onga oyamba aja, nukwere kuno kwa Ine m’phiriumu, nudzipangire likasa lamtengo. 2 Ndipo ndidzalembera…