Danieli 11
1 Ndipo ine, caka coyamba ca Dariyo Mmedi, ndinauka kumlimbikitsa ndi kumkhazikitsa. 2 Ndipo tsopano ndikufotokozera coonadi. Taona, adzaukanso mafumu atatu m’Perisiya, ndi yacinai idzakhala yoletnera ndithu yoposa onsewo; ndipo…

Nthawi ya cimariziro, mau otsekedwa 1 Ndipo nthawi yomweyi adzauka Mikaeli kalonga wamkuru wakutumikira ana a anthu amtundu wako; ndipo padzakhala nthawi ya masautso, siinakhala yotere kuyambira mtundu wa anthu…