Cibvumbulutso 11
Mboni ziwirt 1 Ndipoanandipatsa ine bango ngati ndodo, ndikuti, Tanyamuka, nuyese Kacisi wa Mulungu, ndi guwa la nsembe, ndi iwo akulambiramo. 2 Ndipo bwalo la kunja kwa Kacisi ulisiye padera,…
Mboni ziwirt 1 Ndipoanandipatsa ine bango ngati ndodo, ndikuti, Tanyamuka, nuyese Kacisi wa Mulungu, ndi guwa la nsembe, ndi iwo akulambiramo. 2 Ndipo bwalo la kunja kwa Kacisi ulisiye padera,…
Za mkazi ndi cinjoka 1 Ndipo cizindikilo cacikuru cinaoneka m’mwamba; mkazi wobvekedwa dzuwa, ndi mwezi ku mapazi ace, ndi pamutu pace korona wa nyenyezi khumi ndi ziwiri; 2 ndipo anali…
Cirombo cakuturuka m’nyanja 1 Ndipo ndinaimirira pa mcenga wa nyanja. Ndipo ndinaona cirombo cirinkuturuka m’nyanja, cakukhala nazo nyanga khumi, ndi mitu isanu ow iwiri, ndi pa nyanga zace nduwira zacifumu…
Mwanawankhosa ndi oomboledwa ace pa phiri la Ziyoni 1 Ndipo ndinapenya, taonani, Mwanawankhosayo alikuimirira pa phiri la Ziyoni, ndipo pamodzi ndi iye zikwi zana mphambu makumi anai kudza anai, akukhala…
Angelo asanu ndi awiri ndi miliri isanu ndi iwiri 1 Ndipo ndinaona cizindikilo cina m’mwamba, cacikuru ndi cozizwitsa, angelo asanu ndi awiri akukhala nayo miliri isanu ndi iwiri, ndiyo yotsiriza,…
1 Ndipo ndinamva mau akuru ocokera kuKacisi, akunena kwa angelo asanu ndi awiri, Mukani, ndipo tsanulirani kudziko mbale zisanu ndi ziwiri za mkwiyo wa Mulungu. 2 Ndipo anacoka woyamba, natsanulira…
Kupasuka kwa Babulo. Cirombo cisokeretsa mkazi wacigololo 1 Ndipo anadza mmodzi mwa angelo asanu ndi awiri akukhala nazo mbale zisanu ndi ziwiri, nalankhula ndi ine, nanena, Idza kuno, ndidzakuonetsa citsutso…
Kupasuka kwa Babulo. Maliro pa dziko lapansi 1 Zitatha izi ndinaona mngelo wina wakutsika m’Mwamba wakukhala nao ulamuliro waukuru; ndipo dziko linaunikidwa ndi ulemerero wace. 2 Ndipo anapfuula ndi mau…
Kupasuka kwa Babula. Cimwemwe ndi mayamiko m’Mwamba 1 Zitatha izi ndinamva ngati a mau akuru khamu lalikuru m’Mwamba, liri kunena, Aleluya; cipulumutso, ndi ulemerero, ndi mphamvu, nza Mulungu wathu; 2…
Satana womangidwa zaka cikwi 1 Ndipo ndinaona mngelo anatsika Kumwamba, nakhala naco cifungulo ca phompho, ndi unyolo waukuru m’dzanja lace. 2 Ndipo anagwira cinjoka, njoka yakaleyo, ndiye mdierekezi ndi Satana,…