Aroma 11

Mulungu sanataya Aisrayeli onse 1 Cifukwa cace ndinena, Mulungu anataya anthu ace kodi? Msatero ai. Pakuti inenso ndiri M-israyeli, wa mbeu ya Abrahamu, wa pfuko la Benjamini. 2 Mulungu sanataya…

Aroma 12

Kudzipereka nsembe kwa Mulungu 1 Cifukwa cace ndikupemphani inu, abale, mwa zifundo za Mulungu, kuti mupereke matupi anu nsembe yamoyo, yopatulika, yokondweretsa, Mulungu, ndiko kupembedza kwanu koyenera. 2 Ndipo musafanizidwe…

Aroma 13

Kugonjera kwathu kwa akuru 1 Anthu onse amvere maulamuliro a akulu; pakuti palibe ulamuliro wina koma wocokera kwa Mulungu; ndipo iwo amene alipo aikidwa ndi Mulungu. 2 Kotero kuti iye…

Aroma 14

Cipiriro ca pa ofoka 1 Ndipo iye amene ali wofoka m’cikhulupiriro, mumlandire, koma si kucita naye makani otsutsana ai. 2 Munthu mmodzi akhulupirira kuti adye zinthu zonse, koma wina wofoka…

Aroma 15

Kristu citsanzo ca kusamalirana kumene 1 Ndipo ife amene tiri olimba tiyenera kunyamula zofoka za opanda mphamvu, ndi kusadzikondweretsa tokha. 2 Yense wa ife akondweretse mnzace, kumcitira zabwino, zakumlimbikitsa. 3…

Aroma 16

Zolawirana 1 Ndipereka kwa inu Febe, mlongo wathu, ndiye mtumiki wamkazi wa Mpingo wa Ambuye wa ku Kenkreya; 2 kuti mumlandire iye mwa Ambuye, monga kuyenera oyera mtima, ndi kuti…