Afilipi 1
1 PAULO ndi Timoteo, akapolo a Yesu Kristu, kwa oyera mtima onse mwa Kristu Yesu, akukhala ku Filipi, pamodzi ndi oyang’anira ndi atumiki: 2 Cisomo kwa inu ndi mtendere za…
1 PAULO ndi Timoteo, akapolo a Yesu Kristu, kwa oyera mtima onse mwa Kristu Yesu, akukhala ku Filipi, pamodzi ndi oyang’anira ndi atumiki: 2 Cisomo kwa inu ndi mtendere za…
1 Ngati tsono muli citonthozo mwa Kristu, ngati cikhazikitso ca cikondi, ngati ciyanjano ca Mzimu, ngati phamphu, ndi zisoni, 2 kwaniritsani cimwemwe canga, kuti mukalingalire mtima zomwezo, akukhala naco cikondi…
A wacenjeza asatsate alum wi onyenga, Aonetsere zipatso za Mzimu 1 Cotsalira, abale anga, kondwerani mwa Ambuye. Kulembera zomwezo kwa inu, sikundibvuta ine, koma kwa inu kuli kukhazikitsa. 2 Penyererani…
1 Potero, abale anga okondedwa, olakalakidwa, ndinu cimwemwe canga ndikorona wanga, cirimikani motere mwa Ambuye, okondedwa. 2 Ndidandaulira Euodiya, ndidandaulira Suntuke, alingirire ndi mtima umodzi mwa Ambuye. 3 Inde, ndikupemphaninso,…