Aefeso 1
1 PAULO, mtumwi wa Kristu Yesu, mwa cifuniro ca Mulungu, kwa oyera mtima amene ali m’Efeso, ndi kwa iwo okhulupirika mwa Kristu Yesu: 2 Cisomo kwa inu, ndi mtendere wocokera…
1 PAULO, mtumwi wa Kristu Yesu, mwa cifuniro ca Mulungu, kwa oyera mtima amene ali m’Efeso, ndi kwa iwo okhulupirika mwa Kristu Yesu: 2 Cisomo kwa inu, ndi mtendere wocokera…
Cipulumutso cicokera kucisomo 1 Ndipo inu, anakupatsani moyo, pokhala munali akufa ndi zolakwa, ndi zocimwa zanu, 2 zimene munayendamo kale, monga mwa mayendedwe a dziko lapansi lino, monga mwa mkulu…
Cinsinsi ca maitanidwe a amitundu 1 Cifukwa ca ici ine Paulo, ndine wandende wa Kristu Yesu cifukwa ca inu amitundu, 2 ngatitu munamva za udindo wa cisomo ca Mulungucimene anandipatsa…
Umodzi wa iwo a cikhulupiriro 1 Ndikudandaulirani inu tsono, ine wandende mwa Ambuye, muyende koyenera maitanidwe amene munaitanidwa nao, 2 ndi kuonetsera kudzicepetsa konse, ndi cifatso, ndi kuonetsera cipiriro, ndi…
1 Cifukwa cace khalani akutsanza a Mulungu, monga ana okondedwa; 2 ndipo yendani m’cikondi monganso Kristu anakukondani inu, nadzipereka yekha m’malo mwathu, copereka ndi nsembe kwa Mulungu, ikhale pfungo lonunkhira…
1 Ananu, mverani akukubalani mwa Ambuye, pakuti ici ncabwino. 2 Lemekeza atate wako ndi amako (ndilo lamulo loyamba lokhala nalo lonjezano), 3 kuti kukhale bwino ndi iwe, ndi kuti ukhale…