2 Timoteo 1

1 PAULO a mtumwi wa Kristu Yesu mwa cifuniro ca Mulungu, monga mwa lonjezano la moyo wa m’Kristu Yesu, 2 kwa Timoteo, mwana wanga wokondedwa: Cisomo, cifundo, mtendere za kwa…

2 Timoteo 2

1 Ndipo iwe, mwana wanga, limbika m’cisomo ca m’Kristu Yesu. 2 Ndipo zimene wazimva kwa ine mwa mboni zambiri, zomwezi uikize kwa anthu okhulupirika, amene adzadziwa kuphunzitsa enanso. 3 Umve…

2 Timoteo 3

Zoipa zoopsa masiku otsiriza 1 Koma zindikira ici, kuti masiku otsiriza zidzafika nthawi zowawitsa. 2 Pakuti anthu adzakhala odzikonda okha, okonda ndarama, odzitamandira, odzikuza, amwano, osamvera akuwabala, osayamika, 3 osayera…

2 Timoteo 4

1 Ndikucitira umboni pamaso pa Mulungu ndi Kristu Yesu, amene adzaweruza amoyo ndi akufa, ndi pa maonekedwe ace ndi ufumu wace; 2 lalikira mau; cita nao pa nthawi yace, popanda…