2 Samueli 21
Njala m’dziko, cifukwa cace, matsirizidwe ace 1 Ndipo m’masiku a Davide munali odala, zaka zitatu; ndipo Davide anafunsira kwa Yehova. Ndipo Yehova anati, Ndico cifukwa ca Sauli ndi nyumba yace…
Njala m’dziko, cifukwa cace, matsirizidwe ace 1 Ndipo m’masiku a Davide munali odala, zaka zitatu; ndipo Davide anafunsira kwa Yehova. Ndipo Yehova anati, Ndico cifukwa ca Sauli ndi nyumba yace…
Nyimbo yoyamikira ya Davide 1 Ndipo Davide analankhula kwa Yehova mau a nyimbo iyi tsikuli Yehova anampulumutsa m’dzanja la adani ace onse, ndi m’dzanja la Sauli. 2 Ndipo anati:- Yehova…
Nyimbo yotsiriza ya Davide 1 Ndipo mau otsiriza a Davide ndi awa:— Atero Davide mwana wa Jese, Atero munthu wokwezedwa, Ndiye wodzozedwa wa Mulungu wa Yakobo, Ndi mwini masalmo wokoma…
Kuwerengedwa kwa anthu kuwatengera cilango ca Mulungu 1 Ndipo mkwiyo wa Yehova unayakanso pa Israyeli, nafulumiza Davide pa iwo, nati, Muka, nuwerenge Israyeli ndi Yuda. 2 Ndipo mfumu inanena ndi…