2 Samueli 11

Chimo loopsa la Davide 1 Ndipo kunali pofikanso caka, nyengo yakuturuka mafumu, Davide anatumiza Yoabu, pamodzi ndi anyamata ace, ndi Aisrayeli onse; ndipo iwo anasakaza ana a Amoni, naumangira misasa…

2 Samueli 12

Kulapa ndi kulangidwa kwa Davide 1 Ndipo Yehova anatumiza Natani kwa Davide. Ndipo anafika kwa iye nanena naye, Pa mudzi wina panali anthu awiri; wina wolemera, wina wosauka. 2 Wolemerayo…

2 Samueli 13

Chimo loopsa la Amnoni 1 Ndipo kunali citapita ici, popeza Abisalomu mwana wa Davide anali naye mlongo wace wokongola, dzina lace ndiye Tamara, Amnoni mwana wa Davide anamkonda iye. 2…

2 Samueli 14

Abisalomu abwera ku Yerusalemu 1 Ndipo Yoabu mwana wa Zeruya anazindikira kuti mtima wa mfumu unalunjika kwa Abisalomu. 2 Ndipo Yoabu anatumiza ku Tekowa, natenga kumeneko mkazi wanzeru, nanena naye,…

2 Samueli 15

Kupanduka kwa Abisalomu, ndi kuthawa kwa Davide 1 Ndipo kunali, citapita ici Abisalomu anadzikonzera gareta ndi akavalo ndi anthu makumi asanu akuthamanga momtsogolera. 2 Ndipo Abisalomu analawirira, nakaima pa njira…

2 Samueli 16

Davide akomana ndi Ziba. Simeyi amtukwana 1 Ndipo pamene Davide anapitirira pang’ono pamutu pa phiri, onani, Ziba mnyamata wa Mefiboseti anakomana naye, ali nao aburu awiri omanga mbereko, ndi pamenepo…

2 Samueli 17

Ndipo Ahitofeli ananena ndi 1 Abisalomu, Ndiloleni ndisankhe tsopano anthu zikwi khumi ndi ziwiri, ndipo ndidzanyamuka usiku womwe uno ndi kulondola Davide; 2 ndipo ndidzamgwera ali wolema ndi wofoka, ndi…

2 Samueli 18

1 Ndipo Davide anawerenga anthu amene anali naye, nawaikira atsogoleri a zikwi ndi atsogoleri a mazana. 2 Davide natumiza anthu atawagawa magulu atatu, gulu limodzi aliyang’anire Yoabu, lina aliyang’anire Abisai,…

2 Samueli 19

Yoabu adzudzula Davide 1 Ndipo anauza Yoabu, Onani mfumu irikulira misozi, nilira Abisalomu. 2 Ndipo cipulumutso ca tsiku lila cinasandulika maliro kwa anthu onse; pakuti anthu anamva kuti, Mfumu iri…

2 Samueli 20

Mpanduko ndi imfa ya Seba 1 Ndipo kudangotero kuti pamenepo panali munthu woipa, dzina lace ndiye Seba mwana wa Bikri Mbenjamini; naliza iye lipenga, nati, Ife tiribe gawo mwa Davide,…