2 Samueli 1

Amuuza Davide za imfa ya Sauli 1 NDIPO kunali atamwalira Sauli, pamene Davide anabwera atawapha Aamaleki, ndipo Davide atakhala ku Zikilaga masiku awiri; 2 pa tsiku lacitatu, onani, munthu anaturuka…

2 Samueli 2

Davide alowa ufumu wa Yuda 1 Ndipo zitatha izi Davide anafunsira kwa Yehova nati, Kodi ndikwere kunka m’mudzi wina wa Yuda? Ndipo Yehova ananena naye, Kwera. Davide nanena naye, Ndikwere…

2 Samueli 3

1 Ndipo panali nkhondo nthawi yaitali pakati pa nyumba ya Sauli ndi nyumba ya Davide. Koma Davide analimba cilimbire, ndi nyumba ya Sauli inafoka cifokere. Ana obadwira Davide ku Hebroni…

2 Samueli 4

Isiboseti aphedwa, Davide alanga omupha 1 Ndipo pamene Isiboseti mwana wa Sauli, anamva kuti Abineri adakafera ku Hebroni, manja ace anafoka, ndi Aisrayeli onse anabvutika. 2 Ndipo Isiboseti, mwana wa…

2 Samueli 5

Mafuko onse abvomereza Davide mfumu yao 1 Pomwepo mafuko onse a Israyeli anabwera kwa Davide ku Hebroni, nalankhula nati, Taonani, ife ndife pfupa lanu ndi mnofu wanu. 2 Masiku anapitawo,…

2 Samueli 6

Atenga likasa la Mulungu ku nyumba ya Abinadabu 1 Pambuyo pace Davide anamemezanso osankhika onse a m’Israyeli, anthu zikwi makumiatatu. 2 Ndipo Davide ananyamuka, namuka nao anthu onse anali naye,…

2 Samueli 7

Mulungu salola Davide ammangire nyumba 1 Ndipo kunali pakukhala mfumuyo m’nyumba mwace, atampumulitsa Yehova pa adani ace onse omzungulira, 2 mfumuyo inanena ndi Natani mneneriyo, Onani ndirikukhala ine m’nyumba yamikungudza,…

2 Samueli 8

Davide agonjetsa amitundu ena 1 Ndipo m’tsogolo mwace Davide anakantha Afilisti, nawagonjetsa; Davide nalanda mudzi wa Metege Ama m’manja mwa Afilisti. 2 Ndipo anakantha Amoabu nawayesa ndi cingwe, nawagonetsa pansi;…

2 Samueli 9

Davide acitira Mefiboseti mwana wa Jonatani cifundo 1 Ndipo Davide anati, Kodi atsalako wina wa nyumba ya Sauli, kuti ndimcitire cifundo cifukwa ca Jonatani? 2 Ndipo panali mnyamata wa m’nyumba…

2 Samueli 10

Davide akantha Aamoni ndi Aaramu 1 Ndipo kunali zitapita izi, mfumu ya ana a Amoni inamwalira, ndipo Hanuni mwana wace anakhala mfumu m’malo mwace. 2 Ndipo Davide anati, Ndidzacitira Hanuni…